kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

trappy beats,quest (mw),zeze kingston – ndalama remix كلمات اغاني

Loading...

[intro]
aseh trappy!

[chorus :trappy beats]
ndakuthela ma plan (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?)
kodi nnalakwa chani? (kuchulusa) (kuchulusa) (kuchulusa)
miseche ndizi nkhani (chif_kwa cha) (chif_kwa cha!) (chif_kwa cha!)
ndalama ndalama (aah aah ah)

[verse 1:quest]
mpaka akudana nane akuyesa ndili ndi ndalama
man muzingo hasser hasser basi
nkhani nde ndikungoyika calm
mene ndikuspendela sindingakuwuze
mene tukazisaka sindinakuwuze
ngati ulibe sungandiuze
ndi kale ndinadandaula kuti life ikuyenda slow_mo
ine ayi ndili mkati momo
because i be spending like jomo
ndalama ndi nsamo
olo andinyoze, andikambe, andiseke ine vibe ndi hundrede
olo andihate ine chete ma plan agona pa mandede
[chorus: trappy beats & zeze kingston]
ndakuthela ma plan (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?)
kodi nnalakwa chani? (kuchulusa) (kuchulusa) (kuchulusa)
miseche ndizi nkhani (chif_kwa cha) (chif_kwa cha!) (chif_kwa cha!)
ndalama ndalama (aah aah ah)
ndakuthela ma plan (ndipange bwanji?) (ma plan) (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?)
kodi nnalakwa chani? (kuchulusa) (kuchulusa) (kuchulusa)
miseche ndizi nkhani (ayo trappy!, tiyeni!)(chif_kwa cha) (chif_kwa cha!) (chif_kwa cha!)
ndalama ndalama (tiyeni!, tiyen!,tiyeni! eish!)
ndalama ndalama (aah aah ah)

[verse 2: zeze kingston]
zibwana ndimapanga (zibwana ndimapanga)
posaka ndalama (posaka ndalama)
zibwana sitipanga (zibwana sitipanga)
posaka ndalama (posaka ndalama)
ndiye ndiwe ndani? umatani?
usandipatse busy
dzina ndani? umatani?
usandipatse busy
ndiwe ndani? umatani?
usandipatse busy
dzina ndani? umatani?
usatipatse busy
eish!
[bridge: trappy beats & zeze kingston]
maluzi maluzi maluzi
maluzi maluzi maluzi (musiye mzako)
maluzi maluzi maluzi
maluzi maluzi maluzi (ooh musiye mzako) (m’siye nzako)
maluzi maluzi maluzi
maluzi maluzi maluzi (musiye mzako) (eish!!)
m’siye nzako
maluzi maluzi maluzi
maluzi maluzi maluzi
m’siye nzako

[pre_chorus :trappy beats]
ndakuthela ma plan(maluzi maluzi maluzi)(maluzi maluzi maluzi)
kodi nnalakwa chani (maluzi maluzi maluzi) (maluzi maluzi maluzi) (m’siye nzako)
ndakuthela ma plan (maluzi maluzi maluzi) (maluzi maluzi maluzi)
kodi nnalakwa chani (maluzi maluzi maluzi) (maluzi maluzi maluzi) (m’siye nzako)
ndalama ndalama
maluzi maluzi maluzi m’siye nzako

[chorus: trappy beats]
ndakuthela ma plan (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?)
kodi nnalakwa chani? (kuchulusa) (kuchulusa) (kuchulusa)
miseche ndizi nkhani (chif_kwa cha) (chif_kwa cha!) (chif_kwa cha!)
ndalama ndalama (aah aah ah)
ndakuthela ma plan (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?)
kodi nnalakwa chani? (kuchulusa) (kuchulusa) (kuchulusa)
miseche ndizi nkhani (chif_kwa cha) (chif_kwa cha!) (chif_kwa cha!)
ndalama ndalama (aah aah ah)

كلمات أغنية عشوائية

اهم الاغاني لهذا الاسبوع

Loading...