kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

sevenomore (mw) – palowa njoka كلمات اغاني

Loading...

[pre_chorus]
yah, palowa njoka pano ndiye mkundifunano
palowa njoka pano ndiye mkundifunano
dzuloli mwandithila thope pakanjinga kanu
dzana dz_n_li munangondidutsa pakanjale kanu (palowa njoka)

[chorus]
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka

[verse 1]
amakufuna zikakhalatu zawavuta (yah, yah, yah, yah)
yah, amakufuna zikakhalatu zawathina (yah)
yah, koma ku party umva asabwere amene aja ndachamba
koma ku ukwati umva asabwere amene aja ndamowa (oh my god)

[pre_chorus]
yah, palowa njoka pano ndiye mkundifunano
palowa njoka pano ndiye mkundifunano
dzuloli mwandithila thope pakanjinga kanu
dzana dz_n_li munangondidutsa pakanjale kanu (palowa njoka)
[chorus]
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka

[verse 2]
yah, amafuna uzivutika
amafuna uzingopempha
amafuna uzisawuka
inenso ndekha ndisamapushe, yah, yah
pano p_n_lowa njoka
ka banja kajaso kanatha, p_n_lowa njoka (palowa njoka)

[chorus]
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka
[outro]
yah, yah, yah, yah, yah
yah, yah, yah, yah, yah
panopa p_n_lowa njoka
p_n_lowa njoka
p_n_lowa njoka
p_n_lowa njoka
panopa p_n_lowa njoka
p_n_lowa njoka
p_n_lowa njoka
p_n_lowa njoka
p_n_lowa njoka
panopa p_n_lowa njoka, rr
yah, yachina seven adah

كلمات أغنية عشوائية

اهم الاغاني لهذا الاسبوع

Loading...