kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

seven-o-more – zonsezi كلمات اغاني

Loading...

[intro]
yah
ya achina seven adah

[chorus]
ambuye amatikonda (yah)
mulungu amatikonda (yah)
chauta amatikonda (yah)
ambuye amatikonda (yah)
amatidzutsa tikagwa
amatichilitsa tikadwala
timuyimbile kuti izi_pitilile

[verse 1]
ambuye amakonda aliyense
mphepo imapeza aliyense
mvula imagwera denga la aliyense
dzuwa limapeza aliyense (yah)
onani munthu, onani mbuzi, onani nkhuku, mwanapiye, khwiyo
onani dzuwa, onani mwezi, chiphariwari khakhakhakhakha
_n_lenga zonsezi (yah)
_n_lenga nyanjazi (yah)
_n_lenga nyamazi (yah)
_n_lenga chambachi (yah)
ngakhale mdima ungakure bwanji padziko lapansi kunja k_machabe
ngakhale mvula ingavumbe bwanji padziko lapansi nyerere sizifa
_n_lenga manyazi (yah)
_n_lenga nsanjezi (yah)
_n_lenga nkhawazi (yah)
_n_lenga imfayi (yah)
_n_lenga chisoni (yah)
_n_lenga misozi (yah)
_n_lеnga chikondi (yah)
_n_lenga mtenderе (yah)
_n_lenga satana (yah)
anthu m’matsapana (yah)
anthu m’mangophana (yah)
ana ajaja wa (phrr)
[chorus]
ambuye amatikonda (yah)
mulungu amatikonda (yah)
chauta amatikonda (yah)
ambuye amatikonda (yah)
amatidzutsa tikagwa (yeah_yeah)
amatichilitsa tikadwala (yah_yah)
timuyimbile kuti izi_pitilile

[verse 2]
yah, yah, yah, yay, yah, yah, yah, yah
yah_yah, yah_yah, yah_yah, yah_yah
chopangidwa padziko lapansi, chimathela pa dziko lapansi
nkango wayuda sangalore, mpaka tsiku lina tizayimba__
mtendere (yah), mtendere (yah), padziko lapansi (yah)
yesu ndi mfumu yathu, ndi mfumu ya mtendere (oh my god, oh my god, oh my god)
mtendere (yah), mtendere (yah), padziko lapansi (yah_yah)
yesu ndi mfumu yathu, ndi mfumu ya mtendere, eh (oh my god, oh my god)
(yah, yah)

كلمات أغنية عشوائية

اهم الاغاني لهذا الاسبوع

Loading...