kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

rills – mama كلمات اغاني

Loading...

hook: rillz;

dear mama dear mama
pray for me dear mama
dear mama dear mama
i just wanna a better no drama

verse: rillz;

kuskippa class then kubuka session
ine mu studio anzanga akugela malesson
school ndimafuna kupanga quit
ndikamamva nyimbo zanga ziku hitta mu street
mama mwana wanu ndiwaluso
ndimawayankha mu nyimbo everytime akandifunsa mafunso
ndimabwera mwa mphamvu kuposa mwala wapa legeni
k_mveka area 7
ndimvekenso ku durban
oh my god mulungu watsekula nkh0m_ coz ndinanena odi
politics sindipanga koma chomwe ndafuna ndimachipanga afford
ndikakhala ndimagwetsa msonzi
mzelu zimayima ngati ndili pa pause
nde ndimagwada kupephela kwa mulungu w_nga modzi
nde ndimamuuza what i want
what i want?? wanna achive my goals
hook: rillz;

dear mama dear mama
pray for me dear mama
dear mama dear mama
i just wanna a better no drama

verse: rillz;

you better pay attention
ndikuuze chaka chomwe ndinayamba kubooker session
inali 2017
nthawi imeneyo ndili ndi mzaka 13
oh yes hip hop
ndisanayambe kusipa liqour
flow yanga inali sicker
amanditcha rapper the coolest n_gga
ndisanayambe ma nip
ndisanayambe kukonda ma hip
koma ndinali ndi chick ndimagodya ma lip
asanayembe kukwela ma whip
mkazi ndimakukonda za deep
ati amuna ndi agalu
ananditaya ndinavina ndekha kw_ngwaru
anandisiya coz ndinalibe dollar
kundi blocker
kusiya kundicaller
pano ndikusaka dollar
coz am tryana get rich versace
dream yanga kuyipanga catch
hook: rillz;

dear mama dear mama
pray for me dear mama
dear mama dear mama
i just wanna a better no drama

كلمات أغنية عشوائية

اهم الاغاني لهذا الاسبوع

Loading...