kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

phyzix – wife material كلمات اغاني

Loading...

[verse 1: phyzix]
ndinapeza chi bhebhi anthu adziwe
sindimachibisa sichapadziwe
yemwe zik_muwawa adhiwe
koma ichichi ndichanga chilindiwe
sichingadzakupatse mphindi iwe
chimakhala chili ndine udzimva iwe
vito lake iweyo kudzimwa iwe
umangogwila akaza openga ma byzwe
za ife ndizokoma zothila kale
sitimvetsana kuwawa, tsabola wa kale
uyuyu ndi w_nga si temporary
ndikanena kuti ndimug_ya simphale
kutentha ngati nali samalani abale
akusungila shuga onyambititsa mbale
mkazi uyu ngoyiwalitsa abale
amakomedetsa ngati anthu andale
very good, very good

[chorus: pon g & phyzix]
mamie ndinu chi mkazi chowoneka bho
mumachita kukhalangati a m’video
mamie muli pure ngati kavitiko
mukadzafuna banja ife tilipo
ndinu wife material, ‘terial, ‘terial
wife, ti_ti, ti_ti
wife material, ‘terial, ‘terial
wife, ti_ti, ti_ti
[verse 2: phyzix]
ichi ndichindiwo koma si mpilu
sindinachite kuchiba koma ndichi_deal
ichi ndichibhebhi chadzadza feel
dzina lake ndinaliyika kale pa wheel
chimandik_mbutsa [?]
ma hope anga aku primary ku mphungu
tili ma nfana oyankhula chizungu
she had a chocolate skin, ndimamufila khungu
chibhebhi changachi chandipatsa khungu
ndikayenda ntaunimu sindiwona buthu
ndadwala chikondi teni pa teni
chachita kundifika penpeni
ndavomela mamie ndimalizeni
sindipempha kuti “ambuye ndichilitseni”
izi sizagulu, sizam’memo
ineyo ndili momo m’menemomo

[chorus: pon g & phyzix]
mamie ndinu chi mkazi chowoneka bho
mumachita kukhalangati a m’video
mamie muli pure ngati kavitiko
mukadzafuna banja ife tilipo
ndinu wife material, ‘terial, ‘terial
wife, ti_ti, ti_ti
wife material, ‘terial, ‘terial
wife, ti_ti, ti_ti
[verse 3: pon g & phyzix]
girl you de wife material
i just wanna make you my wife_oh
girl you de one in a million
this feeling for you i can’t deny
iwe ndiwe mkazi wowoneka bho
wowoneka bho, wowoneka bho
iwe ndiwe chi mkazi chowoneka bho
chowoneka bho, chowoneka bho
iwe ndi mkazi o_fitter bho
o_fitter bho, o_fitter bho
iwe ndichi mkazi cho_fitter bho
cho_fitter bho, cho_fitter bho

[chorus: pon g & phyzix]
mamie ndinu chi mkazi chowoneka bho
mumachita kukhalangati a m’video
mamie muli pure ngati kavitiko
mukadzafuna banja ife tilipo
ndinu wife material, ‘terial, ‘terial
wife, ti_ti, ti_ti
wife material, ‘terial, ‘terial
wife, ti_ti, ti_ti

[outro: pon g & phyzix]
ayi, ah (ayi, kolokoto)
mutu w_nga zwe (kolokoto)
very good, very good
very good, very good

كلمات أغنية عشوائية

اهم الاغاني لهذا الاسبوع

Loading...