kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

ndinezulu – tiyenda kuti? كلمات اغاني

Loading...

[intro]
ndinezulu, ts your boy 4.1.3
yeah

[bridge]
ma fella bankala che brutal
ulazo nawemve swokamba
chi chalo chayipa chalula chasasa
ma fella bankala che mbava kulibe afuna kubaza
kubaza bafuna che starter
pa n’drama bengangu bamafa manje iwe nifunseko
tiyenda kuti?

[hook]
tiyenda kuti? nati tiyenda kuti?
vichitika masiku ano nivo desa nkawa nati tiyenda kuti?
tiyenda kuti? zulu nati tiyenda kuti?
ne mwana mungono nasoba nifunseko njila koenda nikuti?

[verse 1]
ma gello bachilamo kusamvela
balli naemve ndiye mbala
chalo chayipa chalula chasasa chaola
ma fella bankala che mbava
kulibe afuna kubaza
no money more money in our pockets
boma inati laya
literally they lied to us anyway
ma fella bankala che mbava baleko nosamba
uwana be pondo wangena screw driver mbombasa
ka knife mu stoga altezza na verve mutumba
kambwili fosholo sbafuno vigwila
nichi-one bad olo paskena pemve sibatacha
banankala chabe ba-junkie panyumba napo banataba kudala
makolo pabondi balemo embekeza
mu- queen ni daily kulila asamba misozi ambuye kodi
ninalakwila pati? pamene machimo yanga yanipeza lelo
nipempa nagwada nalila nalema misozi zanga muzione
munanena kuti nikapempa muzati yanka

[bridge]
ma fella bankala che brutal
ulazo nawemve swokamba
chi chalo chayipa chalula chasasa
ma fella bankala che mbava kulibe afuna kubaza
kubaza bafuna che starter
pa n’drama bengangu bamafa manje iwe nifunseko
tiyenda kuti?

[hook]
tiyenda kuti? nati tiyenda kuti?
vichitika masiku ano nivo desa nkawa nati tiyenda kuti?
tiyenda kuti? zulu nati tiyenda kuti?
ne mwana mungono nasoba nifunseko njila koenda nikuti?

[verse 2]
takonda namfuti takonda namfuti nafuti
vif-kushi vosazibika bwino ndiye vazula k-mitima nati
tasoba chikondi tasoba chikondi ise
tivomo paya muzatu pali nkani yakan’gono nkani yachuma
(imwe)
badangwaleza ndiye baja bene bajubiwa manja na mendo
kapena ni umphawi wamene ulengesa zichitidwe zau satana
sindinga ziwe mwina ndi ndale koma bantu tayuma mitima
ma cadre nibaja bamene bamenya banzao pa vintu ve vilibe pindu
cif-kwa sanavale skipper yene mufuna ninshi afola nthimbo?
ndise bamozi tivutika bonse
manje nichani tinkalila so?
milandu za gbv zingo pakilako ziko latu ino ifuna imwe
ambuye k-mwamba tithandizeni cif-kwa chilungamo nchoti tasoba

[bridge]
ma fella bankala che brutal
ulazo nawemve swokamba
chi chalo chayipa chalula chasasa
ma fella bankala che mbava kulibe afuna kubaza
kubaza bafuna che starter
pa n’drama bengangu bamafa manje iwe nifunseko
tiyenda kuti?

[hook]
tiyenda kuti? nati tiyenda kuti?
vichitika masiku ano nivo desa nkawa nati tiyenda kuti?
tiyenda kuti? zulu nati tiyenda kuti?
ne mwana mungono nasoba nifunseko njila koenda nikuti?

كلمات أغنية عشوائية

اهم الاغاني لهذا الاسبوع

Loading...