kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

molto zambia – rise كلمات اغاني

Loading...

intro:
aise umoyo uyu nje!
ayi nthawi zina zinthu zima pita mu malo mwake
koma eissh.. nthawi zina nde!
ayi koma a yehovah ati sunga
yeah ati sunga!

chorus:
i will rise i will fight
i will keep moving
with the lord on my side
with the lord on my side x2

verse
ye!
july 24th, mwana wa licha ndi eness wabadwa pompo /
kunali cisangalalo konko adakwanilitsa cinthu cinali ngati ciloto/
a damucha maxwello lomba ajambula ma nyimbo anthu amamucha molto/
za umoyo w_nga ndi banja langa conde ambuye mundi sungileko/

tsono i got so many struggles fought so many battles sindi ngakane ayi ena ndimagonja /
i keep going back to my vomits ndi bweleleko ku masanzi anga ayi ena sinimakonza/
got so many addictions mu umoyo i can’t do this si wenye ayi sindinama boza /
kulibe ndi nga uze aliyense anzanga andi seke nawo makolo ni maloza /

pakuti pa ndekha sindi ngathe /
ndidalira inu mutangate /
olefa ndi omega ndinu ndipempha nthawi zonse you see me fall mundi kate /
malipiliro a chimo ndi imfa /
tsono ku kamba pa imfa ayi cimandiwawa/
ndine muntu wama chimo that i don’t deny /
koma being defined by sin a mesiya ayi /
conde we lost so many souls ambiri saw how many we lost talema nayo maliro/

ku k_mbukira zonse zakudala /
yehovah zingatheke ku bweza zakudala? /
mukhululukire onse amambala /
conde muchiritse onse mu vipatala /

chorus:
i will rise i will fight
i will keep moving
with the lord on my side
with the lord on my side

i will rise i will fight
i will keep moving
with the lord on my side
with the lord on my side

i will rise i will fight
i will keep moving
with the lord on my side
with the lord on my side
i’ll move i’ll move
i’ll move i’ll move
i’ll move, with the lord on my side
with the lord on my side!

كلمات أغنية عشوائية

اهم الاغاني لهذا الاسبوع

Loading...