kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

mista gray – munthu wamba كلمات اغاني

Loading...

verse 1
am a low g ngati hippo
ahh (eya tilipooooo)
peculiar people
nyali yapadziko sindichita mantha ndipo/
ndimadziwa christu yesu _n_lipila dipo/
sine wagwamba opanda g
sinditekeseka nnaima pa mtanda nji
namondwe chilala
ife, sitiima ngati ilala
zapadziko ndi zinthu zopanda phindu
sife michira ndife mitu ndithu
ndikuuzilenitu kuli christu ndi kwithu

ndima gainer confi nkati bible ndiphande
nkona pakamwapa pakula ngati chipande
kuspita zokomaku tafuna ngati dandy
sitinyinyilika monga ku ntchito pa monday

mboba ! odzodzedwa ndi mzimu osati komba
sober ! ehh ndili pa duty ndine khobha
zoba! ndimafuna pa den chamma 4 bar
wathu udobadoba sitivalila zigoba

chorus
a mi di eagle mi fly
greatness run inna mi blood
son a god heaven a min yard
mi a salty mi a gwan season di eath
koma sine (munthu)
koma sine (wamba)
moyo w_nga opanda malire
koma sine (munthu)
koma sine (wamba)
moyo w_nga opanda malire

sindingadzale chimanga ndikukolola tomato
kuti uyende upalase life ili ngati bwato
kugwa kudzuka kuyamba k_menya battle
ambuye akuti tidzaponda zinkhanila ndi nsato

opondeleza pansi mdzikoli achulukamo
ndavala ephesians 6 gospel ndi nsapato
faith ndi chishango, mchuno belt wa chilungamo
mau ake ndilupanga kuphwanya tonse mwatchelato

ukazamva fela ana blacka ndi mmene ndilili ndinadzadzidwa ndi mzimu
ndizinthu zondivuta kukhala gangster sinanga kutsaya kunadzadzidwa ndi chim
kukhala normal nono chi rapper chamakono
pa beat sitisiyapo phazi koma mlomo/
muzazing’ono zikh0m_ zogwesa nkhongono
ndimapinda bondo yesu k_muuza zikomo/
ndi mkokomo waziso tathyola kh0m_
muuze suffi tsono kuti nafe tilimommo

ehhh kukhala kape nthawi zina ndiudolo wazizur

we are di uncommon people
jah jah pickney we nuh lose like steven seagle
all di eyes on wi because wi cyaa be hidden
city pon di hill, eternal life we are given

sine munthu wamba utha kuyesa ndimatamba
ngini yomwe ndimapanga ndiyak_mwamba
high high ngati chamba
to all a dem king and queen wagwan!
alluwa (all who are) nuh cheap something wagwan

chorus

a mi di eagle mi fly
greatness run inna mi blood
son a god heaven a min yard
mi a salty mi a gwan season di eath
koma sine (munthu)
koma sine (wamba)
moyo w_nga opanda malire
koma sine (munthu)
koma sine (wamba)
moyo w_nga opanda malire

كلمات أغنية عشوائية

اهم الاغاني لهذا الاسبوع

Loading...