kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

maskal – samadziwa كلمات اغاني

Loading...

[intro]
oh, lala_lala, lala_lala
oh, lalala, lala_lala_lala, lalala, oh

[verse 1]
ndinak_mana naye _n_li yekha
nthawi nk_mapita tik_macheza
pang’onopang’ono tikudziwana
palibe amadziwa tidzafika pano
mwa iwe ndinapeza mzanga
mdzenje la chikondi ndinagweramo
unandipatsa mtima wako ndisunge
chikhulupiliro unapeza mwa ineyo
lero anthu ayamba kudziwa
akuwona chikondi changa pa iweyo
akuti iwe ndi ine ndife osiyana

[chorus]
koma za chikondi changa (samadziwa)
za mtima mw_nga (samadziwa)
m’maganizo mw_nga (samadziwa)
za nkhawa zanga (samadziwa)
komwe tachokela (samadziwa)
momwe tadutsa (samadziwa)
komwe tikupita (samadziwa)
za nkhawa zanga (samadziwa), oh
[verse 2]
mchikondi chathu tinatsala tokha
tinachisamalira lero chakula
lero maluwa ayamba kuwoneka
ena abwera aponyapo moto
dzulo munabwera ndi chikwanje
lero mwatiponyela minga
khalidwe lanu la mtundu wanji?
ndifunseko mumamva bwanji?
mwatenga zoyipa zones
kuvindikila chikondi chathu
nk_mati ndife osiyana

[chorus]
za chikondi changa (samadziwa)
oh (samadziwa)
za mtima w_nga (samadziwa)
maganizo w_nga (samadziwa)
nkhawa zanga (samadziwa)
oh (samadziwa)
momwe tadutsa (samadziwa)
komwe tachokela (samadziwa)

[bridge]
oh, samadziwa, sangadziwe
oh, lala_lalala, lala_lala
[chorus]
za chikondi changa (samadziwa)
za mtima mw_nga (samadziwa)
maganizo anga (samadziwa)
nkhawa zanga (samadziwa)
momwe tadutsa (samadziwa)
komwe tikupita (samadziwa)
oh (samadziwa)
eh (samadziwa)
sangadziwe (samadziwa)
samadziwa (samadziwa)
oh (samadziwa)
(samadziwa)
samadziwa (samadziwa)
oh (samadziwa)
(samadziwa)
(samadziwa)

كلمات أغنية عشوائية

اهم الاغاني لهذا الاسبوع

Loading...