kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

kwemogoon – ineyo كلمات اغاني

Loading...

[intro]
[?]

[chorus: kwemogoon & kingdolla]
kakuti kathozipha chif_kwa cha ineyo
geliso kusiya chif_kwa cha ineyo
kathawaso kwawo chif_kwa cha ineyo
kati kathobwera ku show chif_kwa cha ineyo
kakuti kathozipha chif_kwa cha ineyo
geliso kusiya chif_kwa cha ineyo
yeah_ah, kathawaso kwawo chif_kwa cha ineyo
kabwera ku show chif_kwa cha ineyo, yah

[verse 1: kwemogoon & _kingdolla_]
kak_ma talker zosezo, eh
panopa nde tapanga settle, eh
kulimba ntima ngati metal, eh
kufilitsana ngati tomato
kati kagoma nane ndikhale wake boo
ndikafuna ku trapper ndizikatenga ku stu’
tizapange tiana ka jessy ndi ka ju’
nde kamavunga emoji kundiyika mu mood

[chorus: kwemogoon & kingdolla]
kakuti kathozipha chif_kwa cha ineyo
geliso kusiya chif_kwa cha ineyo
kathawaso kwawo chif_kwa cha ineyo
kati kathobwera ku show chif_kwa cha ineyo
kakuti kathozipha chif_kwa cha ineyo
geliso kusiya chif_kwa cha ineyo
yeah_ah, kathawaso kwawo chif_kwa cha ineyo
kabwеra ku show chif_kwa cha ineyo, yah
[verse 2: kwemogoon & kingdolla]
she say she down for mе kathopanga chilichose (chili’, chili’)
olo ‘usiya geli bola ifeyo tikhale tose (eh, eh, eh, eh)
kamafila kwemo no lie
kamandiwuza ngamo each and everyday no lie (no lie)
kakuti sikangandisiye
kangofuna kukhala ndine
ndikamunda kafuna ndikalime
kabweleratu kati kazishala ndine
yah, yah, kangofila star

[chorus: kwemogoon & kingdolla]
kakuti kathozipha chif_kwa cha ineyo
geliso kusiya chif_kwa cha ineyo
kathawaso kwawo chif_kwa cha ineyo
kati kathobwera ku show chif_kwa cha ineyo
kakuti kathozipha chif_kwa cha ineyo
geliso kusiya chif_kwa cha ineyo
yeah_ah, kathawaso kwawo chif_kwa cha ineyo
kabwera ku show chif_kwa cha ineyo, yah

[outro: kwemogoon]
chif_kwa cha ineyo
chif_kwa cha ineyo
chif_kwa cha ineyo

كلمات أغنية عشوائية

اهم الاغاني لهذا الاسبوع

Loading...