kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

kelvin sings – mantha كلمات اغاني

Loading...

verse 1
i made a choice
to sing for you
nnapanga chisankho
choyombila inu baba

had an ident-ty crisis
was a little indecisive
dziko lapansi linditaye
kenako mundiw-nkhe
zofuna zanga mundipase
kenako ndikuthaweni

nd-nkati zizakhala chonchi
mpaka liti abale
chondiopsya ndichimodzi
mulungu atati andiiwale

so i had to change my ways
cause i got numbered days
ndinatenga baibulo
nawelenga ndipo salimo lidati

chorus

nding-yende muchigwa cha nthuzi waimfa sindiopa
(waimfa sindiopa)
w-nkati ali mwaine waposa wakunja
(waposa wakunja) x2
ndeno yahweh poti mukhala nane
ine mantha ndilibe mantha ndilibe

verse 2

kamba ka mantha
uchimo nnaupasa mpata
kusowa bata
muntima mw-nga

but when i read the verses that you wrote
nnapeza mpumulo
chondilimbitsa ntima
nkudziwa kulikonse muli nane ine

ndiopa ndani poti mwini wake wa moyo waine
akonda ine!!!
ndisowa chani poti mwini siliva ndi golide
ali ndi ine!!!

so i just let him manifest
through my words and my works
my talent was a blessing and a curse
friday am in the club
sunday kuyimba ku church

i had to change my ways
cause i had numbers days
nditatenga baibulo
nawelenga salimo lidati

nding-yende muchigwa cha nthuzi waimfa sindiopa
(waimfa sindiopa)
w-nkati ali mwaine waposa wakunja
(waposa wakunja) x2
ndeno yahweh poti mukhala nane
ine mantha ndilibe mantha ndilibe

كلمات أغنية عشوائية

اهم الاغاني لهذا الاسبوع

Loading...