kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

jeg tellem – chasintha nchani ? كلمات اغاني

Loading...

yeyeyeye

zonse zomwe ndinakuchitila
tak_mbukila ndinakupangila
za mu mtima mw_ngamu ndithu
koma iwe sunkandimvetsetsa
nthawi zonse ndikakuyankhula
unkangowona ngati nzocheza
akwanu ankakufunsa
anzako ankatidabwa ah
unkawayankha kuti
ndimakuvutisa
ndinati koma eh eh
koma asisi
musandinyozese
mwina tizingocheza bwa
mesa unkandisizer
unkati ndachepa nazo
mesa sunkandifuna iwe
unkanditchula nchimwene eh
ndeno

chasintha nchani judie
sunkandimvera judie
sunkandifuna judie
ndeno usandibalalitse
chasintha nchani judie
ndikayimba phone judie
unkandidula judie
mesa unkati uli busy
oh noh noh noh noh
ndeno chasintha nchani judie
oh yeah yeah yeah
mesa unkati uli busy
oh noh noh noh
chasintha nchani judie
oh yeah yeah yeah
mesa unkati uli busy

ine ndine odekha
mtima w_nga woleza
zachikondi naleka
poti pano ndinagiver
mpomwe iwe ukubwera
k_mafuna kundiyesa
ati bwanji siticheza
mesa kodi ndinafwifwa
you gave me your heart i sent it back
wasted your time i want it now

chilichonse chomwe nakuchitila
sunkachifuna
vuto si iwe
vuto ndine pomakomedwa
usakonde munthu
kuposa mene akukondela

oh nd_nkakusizer
nkati wachepa nazo
ine sinkakufuna
nkakutchula kuti nchimwene
oh nd_nkakusizer
nkati wachepa nazo
mesa sinkakufuna
nd_nkakutchula nchimwene

chasintha nchani judie
sunkandimvera judie
sunkandifuna judie
ndeno usandibalalitse
chasintha nchani judie
ndikayimba phone judie
unkandidula judie
mesa unkati uli busy
oh noh noh noh noh
ndeno chasintha nchani judie
oh yeah yeah yeah
mesa unkati uli busy
oh noh noh noh
chasintha nchani judie
oh yeah yeah yeah
mesa unkati uli busy
busy yeah

كلمات أغنية عشوائية

اهم الاغاني لهذا الاسبوع

Loading...