kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

crispy malawi – ukununkhila كلمات اغاني

Loading...

[intro : crispy malawi]
yeah, um_
hm, hm, hm haa
malawian
yeah (yeah)
uh

[chorus: crispy malawi]
how many times should i tell you, kuti ndimakufila
ndungofuna tizichiller, ukudripper ndik_mila
fe! fe! fe! fe! ukununkhila

[verse 1: crispy malawi]
ma guy mwandilira
ngati muona chithako muzachigwira
pa corner ndakupanilira, ndak_matilira
sindikutripper yankha text, phone yangothima
bend down ngati ukulima
kuthokaso chilma, ine ndikulima
mmh mh don’t halla please, ndili high ndadya cannabis
ati spe “what is this?”
ndagwira ass koma ndikufuna kiss
been around never miss, ndika blower imakhala kiss
and ndimakhala busy nde usandipatse busy

[chorus: crispy malawi]
ndikuwuze kangati kuti ndimakufila?
ndungofuna tizichiller, ukudripper ndik_mila
fe! fe! fe! fe! ukununkhila
fe! fe! fe! fe! ukununkhila
ndikuwuze kangati kuti ndimakufila?
ndungofuna tizichiller, ukudripper ndik_mila
fe! fe! fe! fe! ukununkhila
fe! fe! fe! fe! ukununkhila

[verse 2: crispy malawi]
uli fly sizofunika visa
life is too short ngati ndi deezer [?]
ndili busy, mindin’ my bihness
makape ali madzi tuwabatiza
we in the cold ngati mu seasons [?]
kavala bumshort ndima lipha
[?]
tili mangochi walkin’ on water, ndungozifila ngati jesus (splash)
feelin’ my ex, chi body cha bho tipange reverse

[chorus: crispy malawi]
ndikuwuze kangati kuti ndimakufila?
ndungofuna tizichiller, ukudripper ndik_mila
fe! fe! fe! fe! ukununkhila
fe! fe! fe! fe! ukununkhila

[verse 3: achina gatta ase, hayze engola & crispy malawi]
yooh
ndikuwuze kangati kuti ndimakufila?
sindinakuwuze dzina, chif_kwa umandidziwa
kaya uli ndi mamuna, ndikungofuna kugwira
zoti sukufuna (mmh), sindikufuna kudziwa (mmh)
tivaye pawiri bwanji panotu pali phokoso
kuvaya pafupi kakungonunkhira ka mafioso (fe! fe!)
kuvaya ku date moti kazidya, busy ndima photo
zonse ndi chabe man bola kugwidwa ndi dolo
(ndikuwuze kangati?)
kodi iwe jameela, tikukufuna ndi angati?
ndikungofuna kudziwa
ine undimvetse ndikamati, hayze akungochilla
unakandifunsa ine ndinakati (mmh hm) ndak_mangilira (mmh)
tik_masula asavutike k_mayankhula (mmh)
ndikudziwa ali ndi freed mfana wopusher (eeh)
ndinamudziwa kale kale ak_mwa shooter
usakhale ngati sukufuna mfana wophula
[chorus: crispy malawi]
ndikuwuze kangati kuti ndimakufila?
ndungofuna tizichiller, ukudripper ndik_mila
fe! fe! fe! fe! ukununkhila
fe! fe! fe! fe! ukununkhila

ndikuwuze kangati kuti ndimakufila?
ndungofuna tizichiller, ukudripper ndik_mila
fe! fe! fe! fe! ukununkhila
fe! fe! fe! fe! ukununkhila

كلمات أغنية عشوائية

اهم الاغاني لهذا الاسبوع

Loading...