crispy malawi – single كلمات اغاني
[chorus]
ndikavunga text umachedwa kuyankha
ukavunga message pompo ndimayankha
ndikaimba phone ngati sukufuna kuyankha
ngati sukufila unaka talka ndizingoyaka
gangster ali single!
bola ndingokhala single
ndizingoimba nyimbo
ya gangster ali single
[verse]
umangot vepi bwanji sungatenge tchuthi
ndagwila phone yako wazizidwa ulibe juzi?
zosathoka zomwe ndalakwisazo ndizachimidzi
ndili serious siza lucious koma play me si jacuzzi
unena bwanji kuti you with me,when u texting other n_ggas
naneso sindingasibise ndatopa with your shenanigans
k_mandiika ntika
koma uli pa nsika
ine ndi business man
zokwera ndimazitsika
mwina ukufuna g wabanja
or ungofuna mwana
koma mnakuuza kale kuti udekhe ndingo hasa
ndiwe mkazi wa trappa
ndizakupasa ma pasa
ndikupasa mapasa
ndizakuoasa mapasa
ndizakupasa mapasa
ukakwiya simandimafila bho ndipange admit
i like it when we cool ngati salifornia breeze
ma babe ena onse basi ndawapanga delеte
pachi g i’m just trynna show you kuti you tha one for me koma
[chorus]
ndikavunga tеxt umachedwa kuyankha
ukavunga message pompo ndimayankha
ndikaimba phone ngati sukufuna kuyankha
ngati sukufila unaka talka ndizingoyaka
gangster ali single!
bola ndingokhala single
ndizingoimba nyimbo
ya gangster ali single
كلمات أغنية عشوائية
- mandroid echostar › mandroid echostar – midnight sun كلمات اغاني
- jayler › jayler – papers كلمات اغاني
- lit wuulvz › lit wuulvz – fee كلمات اغاني
- sha hustle › sha hustle – g way كلمات اغاني
- duke montana › duke montana – no good for me كلمات اغاني
- wahsan › wahsan – forgive myself كلمات اغاني
- austin monette › austin monette – getting tired كلمات اغاني
- high valley › high valley – whatever it takes كلمات اغاني
- mxtvhe › mxtvhe – девкакошка كلمات اغاني
- ali x recording artist › ali x {recording artist} – beast كلمات اغاني