kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

crispy malawi – koma boys كلمات اغاني

Loading...

[intro: crispy malawi]
koma boys
ayo nihilo bring the beat son haha
zomwe imapanga boys ina
isakuone ukuvina
koma ukulira
(hihihhihi)

[chorus: crispy malawi]
kundibela lighter ntakubanditsa(aah) (koma boys)
kundibela phone ntakuyakitsa(aah) (koma boys)
pamaso kuchiller k_mbali ku disser(aah) (koma boys)
kubwera pa den kundikalipitsa(aah) (koma boys)
tisamavetsana kuwawa
tizimvetsana kukoma boys
kuyikana mkati
osakankhirana mpaka ku khoma boys
k_magawanako wezi wezi
osamaphangira boys
slow paced kuvaya ku front
(tsitsa pang’ono)
osathamangira boys

[verse 1 :ace dirty & (crispy malawi)]
kundikweza kuzanditsitsa
mbiri yanga mumayipitsa
mumafuna zabwino zonse zikhale zanu
mukuwona moyo
k_mandiyenda mbali ngati nkhanu
k_mbali muku hater pamaso k_mandisamala
kufuna kulanda mkazi w_nga (koma boys)
kundiponda ka dollar kanga (koma boys)
osakapeza kamtima mumafuna zoyambana
pano ukupanga zanga
pano tinadana
[verse 2: krazie g & crispy malawi]
krazie tsitsi lako walitani?
ukubanda grade yanji?
ma trainer ngati njanji
ungobanda zi mbanji (zi m’banji)
kwa chigulu changa ine ndina lonjeza
tizingoyaka ku chaser ndi kombeza
kona drip yanga ikuteletele
tele tele
tele tele yeahhh
(koma boys)

[chorus: crispy malawi]
kundibela lighter ntakubanditsa (aah) (koma boys)
kundibela phone ntakuyakitsa (aah) (koma boys)
pamaso kuchiller k_mbali ku disser (koma boys)
kubwera pa den kundikalipitsa (aah) (koma boys)
tisamavetsana kuwawa
tizimvetsana kukoma boys
kuyikana mkati
osakankhirana mpaka ku khoma boys
k_magawanako wezi wezi
osamaphangira boys
slow paced kuvaya ku front
osathamangira boys
[outro: crispy malawi]
zomwe imayithoka boys
anyway osamaf__ka boys
[?]
kukakuponya ku falls
(zomwe imapanga boys ina)
(isakuone ukuvina)
(koma ukulira)
(koma boysss)
(koma boysss)

كلمات أغنية عشوائية

اهم الاغاني لهذا الاسبوع

Loading...