
yobezani - ndikuyamika كلمات أغنية
[intro]
classic!
mmm_mm… orama!
yobezani
eeeh!
emmanuel, yeah!
[verse 1: orama]
eeeh! akandiwona
n’takhumudwa n’sakukondwa
k_makondwera iwowa
k_mandijeda iwowa
eeeh! mbuye w_nga ndi mtondo, ndi mtondo, ndi mtondo
tate w_nga ndi leader, ndi leader, ndi leader
tate w_nga ndi leader
ndipo sindidzalira
ndithu sadzandisiya
ine ndikuyamika!
[chorus: orama]
yeah, i gotta be honest
siwina koma inuyo
sin’zitengera chizolowezi
i owe it all to you, lord!
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika
[verse 2: yobezani]
ndilibe chif_kwa chodzitamira
‘cause i know i’m just a product of your grace
chipanda inu bwezi nditataika
no doubt, yeah i coulda been some waste
n’nalawa ubwino wanu
munandigula ndi mwazi n’kundipanga wanu
munandipatsa moyo wina, now i’m brand new
and i’m enjoying its fullness, sorry dan lu
yeah! i acknowledge it’s all you, lord
m’mene n’nali mu dead_end munali clue, lord
ndikupanga sеlf_searching munali google
till i found myself еngulfed in your cool love
ngiyabonga!
[chorus: orama]
yeah, i gotta be honest
siwina koma inuyo
sin’zitengera chizolowezi
i owe it all to you, lord!
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika
[verse 3: emmanuel]
kundiombola m’zikh0m_
adani anatseka, mwanditsegulira kh0m_
nkhawa n’napachika ndimayenda mu zisomo
ndi yesu zonse zinayera n’mwazi osati omo
zomwe mwachita pa moyo w_nga indedi n’zambirimbiri
mwakuza malire anga, ndikundisinthanso mbiri
adani kundipinga n’cholinga choti andikole mu goli
koma munandi_saver m’manja mwawo, munawayika zigoli (haha!)
ndadza pano kunena zikomo
mdalitso wanu umabweretsa bata m’timamo
sindikulabada olo dyabu akoke tsinya
chomwe ndikuchita nkhumupokela chiuta wa ku chanya
[chorus: orama]
yeah, i gotta be honest
siwina koma inuyo
sin’zitengera chizolowezi
i owe it all to you, lord!
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika
كلمات أغنية عشوائية
- punchface - analysis paralysis كلمات أغنية
- tishmal - bodies كلمات أغنية
- juancho marqués - 22/2/22 كلمات أغنية
- walg - zondvloed كلمات أغنية
- halflives - villain (dramatic version) كلمات أغنية
- dundy - woody كلمات أغنية
- charley night - legs كلمات أغنية
- fabiana cantilo - dejá que suba كلمات أغنية
- paulfigga - popular كلمات أغنية
- blijo - tell كلمات أغنية