kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

trappy beats - kulimbikila كلمات الأغنية

Loading...

[intro]
aseh trappy!

[verse 1]
kulimbika tikulimbikila zivute zokha
kukankha nde takankha, si lero lokha
kuyesa kuphusha ngini osaf__ka
step kuponya step tioloka

[chorus]
tizapuma k_mwamba
tizapuma k_mwamba
tizapuma k_mwamba
tizapuma k_mwamba

[verse 2]
kulimbikila chonchi
mpaka masten ayendele benz
kulimbikila chonchi
abale anga asamalipile rent

[chorus]
tizapuma k_mwamba
tizapuma k_mwamba
tizapuma k_mwamba
tizapuma k_mwamba
[verse 3]
kulimbika tikulimbikila, zivute zokha
kukankha nde takankha, si lero lokha
kuyesa kuphusha ngini osaf__ka
step kuponya step tioloka

[outro]
tizapuma k_mwamba
tizapuma k_mwamba
tizapuma k_mwamba
tizapuma k_mwamba

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...