kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

theresa phondo - assurance كلمات الأغنية

Loading...

[verse 1: theresa phondo]
zaka zambiri zatha
iwe ine tikucheza
mphekesela zinkamveka kuti ife ndi chibwezi
koma ife tinkakana
timvekere sizingatheke
iwe ndi ine sitilola

[pre_chorus: theresa phondo]
lero ndatopa ndimafunso omadzifunsa ndekha
ine ndalema ndimafunso ondifunsaso ena
chif_kwa chomwe ndimadziwa nchoti ndimakukonda
chimodzi chomwe n’funa n’dziwe
ndimve pakamwa pako

[chorus: theresa phondo]
ngati umandikondadi ine
umandifunadi ine?
ndimafuna ndidziwe
ndidziwe, ndidziwe
ndimafuna ndidziwe
ndidziwe, ndidziwe
[verse 2: kelvin sings]
nthawi nde ikupita
nkhawa nde zikubwerabe (bwerabe)
chovuta kodi nchani kunena m’mene umamvera, yeah
i need some assurance
munthune ndikukula, yeah
nde tangonena tipange ma plan kuti zinthu zikhala bwanji

[pre_chorus: theresa phondo & kelvin sings]
poti ndatopa ndimafunso omadzifunsa ndekha
ine ndalema ndimafunso ondifunsaso ena
(oh) chif_kwa chomwe ndimadziwa nchoti ndimakukonda
(iwe ndi amene ndimakonda)
chimodzi chomwe n’funa n’dziwe
ndimve pakamwa pako

[chorus: theresa phondo & kelvin sings]
kodi umandikondadi iwe
oh, umandifunadi iwe
ndimafuna ndidziwe
ndidziwe, ndidziwe
ndimafuna ndidziwe
ndidziwe, ndidziwe
oh, umandikondadi iwe?
umandikondadi iwe?
ndimafuna ndidziwe
ndidziwe, ndidziwe
ndimafuna ndidziwe
ndidziwe, ndidziwe
[outro: theresa phondo & kelvin sings]
ndidziwe, ndidziwe, ndidziwe
(patseko assurance)
ndimafuna ndidziwe
ndidziwe, ndidziwe
(munthune ndikukula)
ndidziwe, ndidziwe, ndidziwe
(patseko assurance)
(munthune ndikukula)
ndimafuna ndidziwe
ndidziwe, ndidziwe
(patseko assurance)
(munthune ndikukula)

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...