kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

the holstar - mtendere كلمات الأغنية

Loading...

intro
zina ndine olimba yah

hook
nyumba lopatulidwa lopatulidwa lopanda mtendere mutu wa nyumba n’chito niku moba nakubwelesa kawele
akachokela ku n’chito na ndalama niku fikila ku moba akachokela ku moba nikuza ku nyumba mukuzani sebanya
(nikale bwanji neoo
nikale bwanji ne muchikwati cho panda mtendere ×2)
ooohooohoooh
muchikwati cho panda mtendere

olimba
poni lungula munati mukanipange mfumu kazi
sunu lelo nichani mumanso muchoka twala misozi
(nu lila ine ×2)
makalindwe yanu yandi zuza yandi liza ine
mukafika pa nyumba ana onse apita ku bisama
mu nkalidwe wa choncho ndipo mwandi ine wanikanga
pa chipanda munani sebanya
ulemu bantu sani pasa
chikondi nimami pasa
mwasaka kuchi taya panja
akulu amati mu chikwati niku limbikila kondi mu nkalidwe otelo ti nkale bwanji

hook
holstar
woman and man, they fell in love, it was swift like a feathered dove, thеy took a bow yes they said them vows _ it was so sweet not considеred foul/
manje mwamuna na boza, lyonse lyonse kuba konka/
na mabvuto yabo sibo konka, mwana ana badwa maloza/
the man was just full of just violence, the woman was suffering silence/
everyday getting beat up, alcohol abuse drinking big cups/
chronicles of a broken home, we don’t wanna live like we’re alone/
really men need to do better, when they’re absent pain like abscess/
children growing up bitter, the trash falls from the litter/
sungani chikondi na bana banu, chiwamila galu, noti wa bandzanu/
siti funa va malilo, tifuna mwana wina malizyani/
maluba maluba noti leka nani, a bambo na bana no faka nkani/

hook

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...