kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

suffix (mwi) - si lero كلمات أغنية

Loading...

[intro: suffix]
wazizur

[chorus: driemo]
si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero
si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero

[verse 1: suffix & driemo]
si lero
uluruwu ndiye sukuchoka
cancer yi ngati ndingofa mwina ndizachila koma
si lero
ndaona zinthu ngati doctor
mmanjamu anthu k_mangofa ndufuna ntapuma koma
si lero
i know lero sizingatheke
pa wheelchair pa one day ndizachokapo
inde ngakhale
si lero
masten anga kuli chete
munapita ngati bodza nzakuonaninso ngakhale

[chorus: driemo]
si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero
si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lеro, si lero
[verse 2: suffix]
mufunse driemo
madе it outta ntchisi ena nk_mati si iyeyo
nawenso uzaiphula aise ngakhale si lero
nzothekanso kufa usanaiphulire ndiye moyo
ma funso onse azayankhidwa ngakhale si lero
wina akuyendera manja f_kwa alibe miyendo
amasamala ziweto
suli wekha tiyeko
ikanso ma earphone ndimvetsele mavutowa azatha ngakhale

[chorus: driemo & choir]
si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero
si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero

[outro: kambwiri sisters & driemo]
si lero (and i still believe)
si lero (though not today)
si lero(not today)
si lero (not today)

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغنية الشائعة حالياً

Loading...