kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

suffix (mwi) - kwanu nkwanu كلمات أغنية

Loading...

[intro:]
listen

[verse 1:]
bambo anga ankandikhazika
pansi, ndili mwana wovuta
ndili chakusekondale heee ndisakuganizaso zoyimba
mwana w_nga ndithu kukula
ife taonapo yambili mvula
ndiwe first born ife tikudalila, ukafuntha uzapita mwachangu k_manda
kusukulu komwe uliko, uzik_mbuka komwe uchokela
nanenso nnali ndiazizanga ambili sindziwa komwe _n_lowela

[chorus:]
dziwa dziwa dziwa, mwana w_nga
dziwa dziwa dziwa, mwana w_nga
dziwa dziwa mwana w_nga
dziwa dziwa, mwana w_nga
kwanu nkwanu nkwanu
mwana w_nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w_nga, kwanu nkwanu
mwana w_nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w_nga
heeehhh

[post_chorus:]
hee huhu
hee huhu
hee huhu
hee huhu
[verse 2:]
yea, life sikhala fair
macritisism sabweletsa sheda
aliyense ali nzokonda zake, akadana ndizokonda zako usamawatengela
k_masiyanitsa azako ndiabale
ena utavutika sangathandize m’bale
osamatengeka akamakuchemelera
enawo ukazazizila azakupanga chandamaleee

[chorus:]
dziwa dziwa dziwa, mwana w_nga
dziwa dziwa dziwa, mwana w_nga
dziwa dziwa mwana w_nga
dziwa dziwa, mwana w_nga
kwanu nkwanu nkwanu
mwana w_nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w_nga, kwanu nkwanu
mwana w_nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w_nga
heeehhh

[post_chorus:]
hee huhu
hee huhu
hee huhu
hee huhu
[outro:]
dziwa dziwa dziwa, mwana w_nga
dziwa dziwa dziwa, mwana w_nga
dziwa dziwa mwana w_nga
dziwa dziwa, mwana w_nga
kwanu nkwanu nkwanu
mwana w_nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w_nga, kwanu nkwanu
mwana w_nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w_nga
heeehhh

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغنية الشائعة حالياً

Loading...