kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

suffix (mwi) - 12 hours كلمات أغنية

Loading...

[intro: suffix]
yo, gd
okay, let’s do this

[verse 1:]
it’s the weekend now, man
tell em it’s the show time
your boy last night couldn’t sleep
pa stage pamandiwopsya
mama tell me, “suffie, wake up”
“pita ukasese panja”
to my fans i’m a servant
and to my parents ndine mwana
ndipupute ka snapback
pa stage pamafunika kutchena
kuzamutuma little sister w_nga
andichapile mphasha
akuti, “sopo njema”
life of an artiste
ndimwe kaye tea ndi bambo
anga ali busy tv ndi politics
akundifunsa, “peter ayimanso?”

[verse 2: suffix]
anyway, madzi ndizithile
koma sayo mphasha sanasite
magetsi athima, pano time ili 12:30
akundikhola ndikamenye soundcheck
ndingovala zina, kukhola mastol azanditenge
number yake ikungoti busy
ndingokwеra minibus, fans yanga ikufika m’ma viwii
ine pansi kuyenda ndi chi mdidi
ndingosiya kuyimba
kenako kuzabampana ndi king
progain anavala ring
swazi suffiе azipsya ntima
njala man, sitinadye nsima
tikhotere kaye pa zodesa
chiyimba chili m’mimba
mfana owotcha nyama kuzandihitta
“ulendo wa k_mwamba unayitha”
“usasiye kuyimba”
tachedwa, bob wayamba kushisha
keep change, wa nyama umayitha
tinalibe yosintha
[interlude: suffix]
alright, tandiponyere phone yo

[verse 3: suffix, with saint realest]
nditcheke pa facebook, ndiwone ma comments
“suffie ndi wa fake, mfanayi akutiwonjeza”
“ayimba bwanji ndi martse? mfana wochimwa ngati amene uja”
“akubeefana ndi gwamba? kapena ndi…?”
kuzatcheka whatsapp, message ya martse
“sorry suffie, mwana, ndakukuzisa fans
dude, i’m only human, sine wa satanic”
i could feel your hurt in the vn that you sent me
then i prayed for his soul and i prayed for the stage
k_mabwera anthu four amafuna ka pic
kuzayima ka pose ndi ka smile ka fake
m’mutumu zinthu thoo mwagozaza ma stress
kuzalandira ka call akuyimba masteni
“mukachoka uko muguleko micheni”
and then comes marumbo with the mic on his hand
akachoka lily, dude you coming on stage
nkuzakwera pa stage ndikukhila ka set
nyimbozi ndi therapy zimakhila ma stress
ma prayer is that you see me as a person
i hurt and i feel i’m not perfect
i’m human
[verse 4: saint realest]
over rise
from one time perfection
over god, i no said to be human is to do wrong
sometimes right to see, to lose sight
to walk in the light and in the dark
with jah love, i reign with more perfection
so we can realize our imperfection
i dip inna we soul but with jehovah we grow more and more
cuh we only human

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغنية الشائعة حالياً

Loading...