suckle - intro lyrics
Loading...
ine ndimagona//
kudzuka osalota//
osamanditchula star sindimafuna kuwala chikoka//
ndimayenda ndicholinga pano ndi abraz//
thupili ndi temple mokhala okhetsa mwazi//
mtendere ndikusangalala zokhaso basi//
ayi njee kugawa mawu ndicholinga chathu//
eeh eya ma guy ndinewakhama ngini zanga zimayenda mwa kaya//
sorry ma guy ndilibe chuma koma za dziko nde zimandig_ya//
zimandinyenya zimandiphwanya//
mtima odzadza ndi dama chandichosera ch_nkhwaya//
awo kaya yesu w_nga wauka//
_n_li ndi mwayi oborna ona pano awutaya kupembedza chauta//
chomwe nnakhazikitsa mu mtima mw_nga inu kaya//
checka boldness ase koma suckle ndiwakhama//
ladies and gentlemen!
welcome to sleep without dreams extended playlist!
كلمات أغنية عشوائية
- z-ro - make it bacc home lyrics
- king 3d - she in her feelings lyrics
- vesku jokinen - enkelin silmin (vain elämää kausi 11) lyrics
- glaceo & pierre leck - unknown lyrics
- kevtopo - ¿compararme pa' qué? lyrics
- nano (jp) - restart lyrics
- sad penny - summertime lyrics
- allebou - lumière bleue lyrics
- fizzy blood - cue to leave lyrics
- kaysia - club27 lyrics