
sagonjah & tadala - zima كلمات أغنية
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf__ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati
[verse 1: tadala]
sindikayika
kuli mtima wako sikutalika
minga yachikondi mayo mtimawu wabayika
nde umaona ngati ndimakusata mapazi
ndikadekha ndekha jenkha manyazi
phone sumandiyankha ndimafoka
ndimafuna pena k_mandikankha
umatalikira
umatayilira
olo namondwe panyanja amakalipira
umandipilira
kupangitsa zinthuzi k_mapitilira
vundula madzi akhoza k_madikira
ndiwe w_nga komabe mtimawu umakusilira
madzi ak_mwa osamapisilira
sanje azikhala nayo mulungu ine ndi nda?
mwina ndikufunika uphungu nde tita?
sanje azikhala nayo mulungu ine ndi nda?
mwina ndikufunika uphungu nde tita?
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf__ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati
[verse 2: sagonjah]
mwina ndi mantha chabe
simmawupeza ndisaname
mwina m’mangawa simnachile ndimilandu yatizibwezi takale
mwina ndi mamuna wansanje
mwina, mwina ndi trauma
chikondi chandiwonetsa zowawa
pano [?] kuteteza mtima w_nga
koma mai mai kalanga
muzitaye zonse ine mmapanga
siine m’ngelo pena ukali
kaduka kuswaya chikondi kutali
koma ngati tingak_mane pakati
tonse tikubwеla kuk_mana mkati
zomwe ndipeleka ndi zomwе ndiyembekeza
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf__ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
[bridge]
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf__ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
كلمات أغنية عشوائية
- bill monroe - the sailor's plea كلمات أغنية
- h y b r i d - formula of fear كلمات أغنية
- sed non satiata - urgent d'attendre كلمات أغنية
- regine velasquez - where are you now كلمات أغنية
- mafia - speed racer كلمات أغنية
- tom paxton - reason to be كلمات أغنية
- hildegard knef - geh fort von hier كلمات أغنية
- american theory - boiling point كلمات أغنية
- tavares - can't get enough كلمات أغنية
- mothersound - hollow heart كلمات أغنية