
ritaa - mubwere lyrics
ritaa mubwere lyrics
oh, sispence, oh oh oh
ritaa.. h_llo?
(verse 1)
munachoka kuti mukukasaka ndalama
mpaka lero simunabwelerenso
munachoka kutisiya ndi amai athu
koma simunabwelere..
simumatumizanso chithandizo kunyumba
koma zoti mukuchita bwino tik_mva
sitimadziwa ngati mumatiganizira
sitimadziwa ngati mumatik_mbukira
(chorus)
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba..
(verse 2)
tinakula, otilera _n_li mai athu
kuvutika pamodzi ndi amai athu
komanso mutangopita
achimwene anatisiya
ana anu akungolira
chilichonse kuvutikira
phone yokha mukanatiimbira (h_llo?)
kalata yokha mukanatilembera (you know)
sitimadziwa ngati mumatiganizira
sitimadziwa ngati mumatik_mbukira
(chorus)
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba
(bridge)
ohh, mubwelere kunyumba
oh, oh , oh ..
mubwelere kunyumba
(chorus)
Random Lyrics
- mr. disappointment - thorns lyrics
- g-mon - different season lyrics
- 2much - check lyrics
- the magic eyes - the know it alls lyrics
- now united - love somebody lyrics
- crude play - i'm ok (괜찮아, 난) (romanized) lyrics
- lil nas x - that's what i want lyrics
- lilgrinch & lil ricey - synergy lyrics
- dyamond doll - automatic lyrics
- sheryl crow - the first cut is the deepest (live from the ryman / 2019) lyrics