
raycot - sungamuwalile lyrics
intro
oooooo sungandiwalile
oooooo sungandiwalile
oooooo sungandiwalile
oooooo sungandiwalile
chorus
sungandiwalile sunga ndi walire ee
sungandiwalile sunga ndi walire ee
sungandiwalile sunga ndi walire ee
sungandiwalire sunga ndi walire ee
verse 1
sungandiwalile olo utachoka kudzuwa
iwe olo usambe kwaine umaoneka wotuwa
kukudya pa beat ndiwe chitumbuwa
sim_th_ kuiba bac mumangodziwa kukuwa
bridge
fanz imandifila ndine mfana ochitisa kasoo
ndachoka kutali ndapanga zinthu zooneka ndimasoo
kuponda ma giya pamtunda motha yopanda olo gasoo
chomwe ndimadziwa ndikuphusha dancehall
chorus
sungandiwalile sunga ndi walire ee
sungandiwalile sunga ndi walire ee
sungandiwalile sunga ndi walire ee
sungandiwalire sunga ndi walire ee
verse 2
i been in a game for long time
n_z_yamba ndili yute
daily kupanga za progress sindikhalaso ndi tchuthi
sungandiwalile olo uyase tourch
lеro ku dropa mawa so kudropa
check on my number sindikuflopa
nakupasa ma flow sonnie ukut chan
mukhumba ka flow еya penjani
i came from the dirty ndi achina shizzo
sungandipeze uotcha diesel
pa 8 19 i was busy to learn
ukupanga lero i’ve done it already
nali ndi ex akut makoma zedi
osandiika pa poster siiwe trynna pay me dawg
كلمات أغنية عشوائية
- corky the juice pigs - psa lyrics
- corky the juice pigs - psycho lyrics
- corky the juice pigs - rabies lyrics
- corky the juice pigs - remember lyrics
- corky the juice pigs - rok stedy lyrics
- corky the juice pigs - skateboard lyrics
- corky the juice pigs - suzanne lyrics
- corky the juice pigs - when the moon lyrics
- corky the juice pigs - the church lyrics
- cormega - 5 for 40 lyrics