rapsean - njinga كلمات الأغنية
song; njinga
artist; rapsean ft bawondage a level music
intro(rapsean)
(koma rapsean adha)ak-malimba ziwindi eti haa
(thama on the beat)k-mavayisa bebi yanga et haa
(a level on this one)ak-mayesa ndizophweka et
(njinga adye basi)hahaa! heeh! adya nazo njinga
njinga x2 adyetsedwa njinga
njinga x2 aikwera njinga
njingax2 inde tati njinga
njingax2 makape adye njinga
verse 1 (rapsean)
yoo ahh
all my life ive been real adha ,kwa mkazi ine sinadyeko njinga adha
ndimagwira akazi ten mfundo imodzi adha, nde wina nk-mayesa angamake adha
yea am crazy but some people stupid,they act n do things without thinking
while they keep talking i keep moving, i leave em behind then i kiss em goodbye yeah
my girl is a goddess,all of these boys do wish they had her all of these boys do wish she knew em
but she don’t knw em ,she don’t wanna know em (ah)
yellow bone skin and pinky lips tho kamkazi kubeba ngati mngelo(uh)
ma yoe ambirimbiri ak-matha kuvaira koma mkaziyu anandikakamira
ofcourse nane nnachitanso kulanda koma sikuti nanu mungalande
mukalimbana naye mukwera njinga mugwanso nayo mungalande
she complicated am complicated,we make a match tiyatsa moto
my god is gracious he gave her me and gave me her, that’s pretty nice
i am nice,i don’t cheat,i just cool down and then take care of her
these pipo not nice ,they making no sense,they go after her while am sleeping with her
na bebi yane tukhala makola, kwe soka kwa mnyake uyo sanje zamukola
ine ni rapsean munthu mukali ,vayila bebi yane machero nkhudindi gadd-mn!!
pre-hook (a level)
huh! wolimbana ndi ife adye njinga
huh! maswazi nonse lero mudye njinga
wozimitsa magetsi naye adye njinga
huh! njinga adyetsedwe njinga(echoed)
chorus(rapsean)
ak-malimba ziwindi eti huh!
k-mavayisa bebi yanga eti huh!
ak-mayesa ndi zophweka et haha
heh! adya nazo njinga
njinga x2 adyetsedwa njinga
njinga x2 aikwera njinga
njingax2 inde tati njinga
njingax2 makape adye njinga
verse 2 (bawondage a level music)
amati ak-maka,amati akutaka,amati afuna alande amati akuhasa
kuvaila tchiki yaine kufuna kuziona udolo kundiona kufatsa
ndinakakhala kuti sinakunegulire oro number sanakakupatsa
koma ngati ukudwala chimfine tchiki yanga usai-etsee!!
yese! ,ukudutsa mpheche mpheche,iwe ndi chitete tete
ngati sugar usandiseketse,ndipo nkhani usapeke
wakwera njinga yakapalasa, ka mtima kakoko nde kalasa
uk-mva kuotcha ngati malasha,iwe mfana khala apa palasa
amaona zophweka amaona zophweka kulanda mkazi
amaona zophweka, amaona zophweka,walemba mmadzi
amaona zophweka amaona zophweka kulanda mkazi
amaona zophweka, amaona zophweka,walemba mmadzi
achule awerenga ah ah,akhw-ngwala akuseka ah ah
ngati player ndakuseka ka ka, ineyo ndakuseka ha ha ha
tchove ngilingili wadya piripiri,muli awiriwiri yada mbirimbiri
njinga ngilingili belu ngilingili,muli awiriwiri wadya ngilingili
pre-hook(rapsean)
haaaaaaaah wolimbana ndi ife adye njinga
ihaa maswazi nonse lero mudye njinga (uh)
wozimitsa magetsi naye adye njinga haaaa
njinga ,adyetsedwe njinga haaaaaaah
chorus(rapsean)
ak-malimba ziwindi eti huh!
k-mavayisa bebi yanga eti huh!
ak-mayesa ndi zophweka et haha
heh! adya nazo njinga
njinga x2 adyetsedwa njinga
njinga x2 aikwera njinga
njingax2 inde tati njinga
njingax2 makape adye njinga
كلمات أغنية عشوائية
- riflesso - xiii كلمات الأغنية
- sluggg - demons كلمات الأغنية
- sonic54 - how ????? كلمات الأغنية
- los jaivas - indio hermano (1997) كلمات الأغنية
- singlikephilly - tired كلمات الأغنية
- sangatsu no phantasia - 群青世界 (cobalt world) كلمات الأغنية
- vicky nhung - màu áo anh hùng كلمات الأغنية
- iona frost - blu كلمات الأغنية
- leyshock - feeling free كلمات الأغنية
- kaeley jade - highway 16 كلمات الأغنية