praise umali - time lyrics
[verse 1]
anzanga ak_mati ndizitolera
ati “i need time”
i need time
i need time
i’m just tryna take it easy, easy
koma mtima umawawabe sometimes, believe me
[pre_chorus]
koma ati zonse zimatha, ma feeling amatha
ingodekha zimatha, dekha zimatha
usalire zimatha, ululu umatha
ingodekha zimatha
chikhala nthawi ndi mankhwala, nkana chila dzana
mwina lakula ndi balali, mtima umawawa
ngati nthawi ndi mankhwala, bwezi ntachila dzana
kapena mwina mawali
[chorus]
komabe mwina i just need time
i need time
ndichila i just need time
i need time
[verse 2]
mwina ndiyese therapy
’cause it’s been a while now since i felt like me
olo ndingodikila (ndingodikila), zikhala better (zikhala better)
usazitengera iwe, ndizamdziko izi
[pre_chorus]
nde ati zonse zimatha, ma feeling amatha
ingodekha zimatha, dekha zimatha
usalire zimatha, ululu umatha
ingodekha zimatha
koma chikhala nthawi ndi mankhwala, nkana chila dzana
mwina lakula ndi balali, mtima umawawa
ngati nthawi ndi mankhwala, bwezi nditachila dzana
kapena mwina mawali
[chorus]
mwina i just need time (maybe i need sometime, i need sometime)
i need time (i need sometime, maybe i need sometime)
ndichila i just need time (i need sometime, i need sometime)
i need time (i need sometime, maybe i need sometime)
[outro]
i need time
i need time
i need time
i need time
كلمات أغنية عشوائية
- elijah the boy - good luck to you lyrics
- 666chainz - dirty white bedroom walls lyrics
- эмелевская - кроссфит lyrics
- gofran lyrics
- serena assumpção & xênia frança - oxum lyrics
- 24hrs - real life lyrics
- maria idol - yang terbaik lyrics
- farah farhanah - bukan sekarang lyrics
- joan idol - jailhouse rock lyrics
- fresco aka yungshangsun - knightslikethis lyrics