
ndinezulu - udani كلمات أغنية
kudabwa
nthawi zina ndima dabwa
w_nga anthu momwe ama khala
kubaba mtima w_nga uma baba
ubaba anthu zomwe ama panga
kudana anthu awa ama dana
sibanja ine mango khala
mwina ndi nyanga zomwe wina ana panga
kapena sinyanga nakuba kapena chabe nikaduka
kamene kalengesa banthu bamozi kupeza vif_kwa
cif_kwa mayeso fufuza koma sina peze cif_kwa eh
kunjako nko kudha macita mantha ndi khalidwe yawa
udani waconco wacoka kuti ma lankhulana
pempelo yanga niyoti izozo ma lalilane
nanga cikondi munali naco cinapita kuti
funso
kudabwa
nthawi zina ndima dabwa
w_nga anthu momwe ama khala
kubaba mtima w_nga uma baba
ubaba anthu zomwe ama panga
kudana anthu awa ama dana
sibanja ine mango khala
k_makhalila midesu
ena akulila yesu
mundisamalile ana banja isa pwasuke tikhale ifeso
ogwilizana despite what we facing i hope we don’t break us ineo
pemphelo yanga ndiyoti udani ulipo kuntima uthepo
koma zukhala nga e sizotheka anthuwa afuna afepo
udani waconco ku opya ambuye k_mwamba muyanganilepo
k_ma kangana pa zopanda phindu poka poka ena afepo
anthu wa ndani aloza umbuli wa conci ine sina onepo
kudabwa
nthawi zina ndima dabwa
w_nga anthu momwe ama khala
kubaba mtima w_nga uma baba
ubaba anthu zomwe ama panga
kudana anthu awa ama dana
sibanja ine mango khala
كلمات أغنية عشوائية
- mike falzone - unsuccessful supervillain كلمات أغنية
- mike falzone - famous كلمات أغنية
- mike gordon - another door كلمات أغنية
- mike gordon - dig further down كلمات أغنية
- mike gordon - radar blip كلمات أغنية
- mike gordon - voices كلمات أغنية
- mike mareen - agent of liberty كلمات أغنية
- mike mareen - dont talk to the snake كلمات أغنية
- mike mareen - love spy كلمات أغنية
- mike ness - all i can do is cry كلمات أغنية