kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

namadingo - maury كلمات الأغنية

Loading...

namadingo
k_mvetsetsana inde tinkamvetsetsana
ija inali true love, tinkakondana ah ah ah
zatsogolo lathu zidali mmanja mwake, mwa mulungu
koma yemwe adanena palibe chosatha
sadanane zonse zimatha ah ah
zimawawa palibe chamuyaya ah ah ah ah
maury adandisiya, maury adakwatiwa

ine zidandiwawa koma (ululu umatha ah ah ah)
pakapita nthawi ine (mabala achila ah ah ah)
maury adandisiya komabe (ululu umatha ah ah ah)
moyo goes on (mabala achila ah ah ah)

palibe chamuyaya
papita nthawi ine, maury atandisiya
maury adakwatiwa
atapita maury nalo dziko lilandikulira
mtima kupweteka nk_mangopirira (kupirira)
pagulu uk_mwetulira k_mbali ukusisima ukulira
maganizo kuk_mbuka momwe chikondi ch_nkakomera
simomwe mtima wako nawonso umawawira
kutopa ndi kulira maso ku fiila
kufuna kudzimangirira ah ah ah
koma ayi ayi uh huh
zonse zimatha mchimwene w_nga
palibe chosatha mchemwali w_nga
zimawawa komabe, ululu umatha ah ah ah
papita nthawi komabe, mabala achila ah ah ah
ine maury adandisiya, komabe ululu umatha ah ah ah
ndipo mabala achila ah ah ah
maury adandisiya, maury adakwatiwa (palibe chosata ah ah ah)
ndipo palibe chamuya ah ah ah
olo ndalama imatha, iwe kukhala mmaludzi
maudindo amatha, iwe kukhala n0body
olo maludzi amatha, mutaipedza bandulo
inu minyama imatha, iwe kupеdza madalitso
ungo limba mtima (moyo ndi choncho moyo oh oh oh)
tsiku lina udzachira (moyo ndi choncho moyo oh oh oh)

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...