mufrika - kumpeta milombe lyrics
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
kuzebenza tisebenza bwino
ndalama timapeza
koma potsilizira pake eeh!
tinali nao anzathu
tinali kuseka nao
tinali nao astikana
odsziba kusamba bwino
nanga lelo alikuti
ambuye mwatisiyiranji
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwsila alumbwana
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwasila alumbwana
iyi nthenda niyoipa
ndiponso siyimasankha
imagwira aliyense
kuyambira kubana mpaka makolo
koma anyamata ndi astikana
nibame bakula maningi
nangatu tizakhala bwanji
popeza ndiye tsogoro
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
كلمات أغنية عشوائية
- ******** [the drink] - kinderpunsch lyrics
- the sea the sea - the match lyrics
- sade cinco - risk lyrics
- capital cities - chasing lyrics
- skyward story - smile lyrics
- spark! (sweden) - chaos lyrics
- martha wash - i've got you lyrics
- anssi kela - kaveria ei jätetä lyrics
- summy - sus lyrics
- brenno - più vicino al sole lyrics