molto - lizu langa كلمات الأغنية
verse1:
abale dzina langa mosabitsa ndine gilibo
ndicokera pamudzi pa maguya pa aphilipo
god has really worked in my life nalelo tilipo
let me take you through my journey achimwene let’s go
makolo anga emwalila pomwe ndinali na zaka khumi
suddenly everything changed n0body cared for me
achi bululu etaluka non remembered me
koma katundu we egraba not shared with me
many times i thought of suicide, kodi ndikhalilanji
eloi eloi! kodi mwandi siilanji
i used to sleep in the streets nimwai kugonela tangy
hoping for the vision like the blind
“kwacha tionenji?”
till one ninakapita kuchalichi kuka preza
oh man i was blessed ndi ma anandi cheza
ninali nkosa yosoba koma ambuye anandibweza
suicidal thoughts mubongo mw_nga anageza
nthawi zina ndika khala nkaganiza ndimalila
zimene andicitila ajehovah nizopambanila
madalitso ndi mbwe obwela ndi opatikizila
he’s a faithful god i believe ndazindikila
my friends you may be living in this same life i was living
kugona mu street everyday that’s were you sleeping
kugo’ona na njala you don’t have anything for eating
remember ambuye sago’ona pali we he’s never sleeping
chorus:
( iyi ndi lizu langa ) x2
iyi ndi lizu langa. this is my voice
verse2:
when i was born nina badwa ndi matenda ochedwa cibwibwi
cingerezi stammering i don’t really speak so clearly
anzanga onse enzo ndiseka ena k_mandicha mbuli
mwina kundipitikitsa kamba kacibwibwi
izi zinali kundi khuza k_m’tima
it bruised my soul mum’tima mw_nga it occupied enterely
nthawi zonse i used to ask my mum why?
ndicif_kwa ninji, this speech disability
kodi mulungu ama kondwa conci
k_mandiona conci, kusebanyika and this pain. kodi?
amai ndiye amene _n_li kundi fungatila
cikawawa maningi _n_li kuti osalila
she one day told me my son god has a plan for you
before you were born ajehovah he already knew you
olo kuyimba kwako uku…
“danka”
mwa chidule, ndikali mwana i used to have dreams of me singing
pakufalitsa uthenga till i joined a competition
during the competition a lot of people got saved
there was a woman who had complications with her pregnancy
koma anapapa safely just after watching me sing
a man in ‘chimbwakaila’ jailed in prison
he gave his life to christ just after watching me sing
mpikitsano ndina wina koma
zinthu ndina phunzira ambuye mungathe kuti satisfaya ndinu nokha
chorus:
( iyi ndi lizu langa ) x2
iyi ndi lizu langa. this is my voice
verse 3:
umoyo w_nga nthawi zina ndima khala so lost
ndika pishamo ink anzanga ma sorrows
okondedwa kupaka pa dziko we’ve lost
anthu tinali nawo k_mwa na kudya pamodzi
why did you leave.. i thought that you’d come back
i waited… i waited!
nthawi zina i wait for you to come from work koma citseko sichi seguka
with my eyes on the door waiting kodi simu segula?
oh sorry i forget nthawi zina ndi maluba
your old memories keep falling in my head nga maluba
since the day muna ndi siya the day you were gone
i asked myself these questions why muna ndi siya alone
ndi mafunso at the back of my head ena opanda pace
makonsho ninali nawo cikanga google siinga yankhe
till i met this so called jesus through the fishers of men
they introduced him to me they said he’ll take all my pain
i was like, ninayesa ivi vina cocaine na mbanje
so you mean this sane jesus aza chotsa ivi manje?
nah..
anzanga kuli ine inali nkhani yoseka
never knew it kuli ambuye zonse ndi zotheka
all the pain and sorrow on me anatenga
yonse ma frasi ndi depression anatenga
olo mabvuto pa thupi alu pweteka
no drug or man can solve it ndi yesu ove yekha only!
chorus:
( iyi ndi lizu langa ) x2
iyi ndi lizu langa. this is my voice
كلمات أغنية عشوائية
- el chojin - p.d. كلمات الأغنية
- bvana iz lagune & mikri maus - antihepi كلمات الأغنية
- nalyd - channel 03 كلمات الأغنية
- dopeworld - money كلمات الأغنية
- ester elias - intuição materna كلمات الأغنية
- the game - the town كلمات الأغنية
- uverworld - rob the frontier كلمات الأغنية
- robyn hitchcock & the venus 3 - ny doll كلمات الأغنية
- beatrice eli - the last time كلمات الأغنية
- xyz1 - xyz كلمات الأغنية