kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

mistah yemie - mistah vs yona كلمات الأغنية

Loading...

[intro]
“you know i’ve been waiting for this moment
talking to my own self”

“telling the new me, i have to keep going
and the old me, not to worry, we doin’ good”
(yeah)

“this is it right now
this is the time
my time is now you know”

[verse 1]
(yeaoh, yeaoh)
dear yona
ndudziwa uli boh
ambili amakufila ndiwe chimfana cha boh
mfana wapa easy wa umunthu ochuluka
okonda aliyese ndi chikondi chosa guga(mhee)

sorry ndine amene ndinakusintha
koma simpanga regret nangoyenera kuchita
zisankho tinapanga ona pomwe tinafika
ngini inasintha now we goin’ up quicker

am sorry pobwera ndinabwera ndima kick(brr)
kuku dyeletsa fees(yeah)
kuku lawitsa nip(yeah)
kuku sweletsa mtima pofuna kulawa lip(yeah)
pano tilibe problem mboni ndi magigi(brr)
pano, makomo kutseguka
ngini ikutheka
chikondi chosaguga
chik_mapezeka
zi dollar unkakhumba
zik_mapezeka
mental kupha ngati nkhumba
zik_mafilika

pano na leaner zochuluka(ooh)
omwe ankaphwekesa pomwe tinkayamba panopa
tinangowa tuluka(prr)
mafana o dissa onyoza kudusa kugwesa
kukhara ngat sulumba(yeah)
maloto omwe tinkawa lota aja ndinangowa
tengera kunyumba(home)
nangowa tengera kunyumba(yeah) yeah

[verse 2]
(yeaoh, yeaoh, yeaoh)
dear mistah
am happy munabwera
when i tell you about my dreams
am happy munavera
when i tell you about the queens
simun_z_ tengera
you were just aiming high kut zizitiyendera
i don’t blame about the fees(prr)
when i look ina your pocket fully green
like di trees(money)
muku pusher be zingini mavuto kupanga
treat(yeah)
kuphulisa ma tune mu ghetto kupanga trend(yeah)
ey, ey

coming from the bottom tikukwanitsa(brr)
k_manena toto zotinamiza(no)
mistah yemie your in total mumakwanisa(yeah, yeah)
ngati skeffa chimoto mumayakisa(phuu)

nd_nkafuna kukhara “lawyer”
koma mu game mutango “lowa”
nduku yamikani “fodya”
poti game mumai “ponya”
simui pho…
mumai oo…
mumai do…
mumai sintha ndikuipanga zimene inuyo mumazi
“lota”

eehhh
mukamakhara osamadanda
mudziwe am so proud pazimene mumapanga
i know nthawi zina mumayaka, mumabanda
but still we gon’ make it atitsogolera jajah
ine yona

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...