
mista gray - yesu كلمات أغنية
verse one (mista gray)
bayete mkosi..!
mfumu yamafumu kalonga (yesu)
alefa ndi omega oyamba ndiotsiliza dziko lonse limachonga (yes)
mpulumutsi yekhayo onditola ndikagwa kundilimbitsa ndikaf–ka kuchimake kwama chilitso
machine opangila machine kuti akapange machine opangila machinenso
akatundu omanga ndima wire
moto buuuu consuming fire
mesiah, mudalipo mulipo ndipo mudzakhala muyaya
mano alikonko mwaika chimwemwe kutsaya(kikiki)
nnampasa zonse andichengete ndili khethekhete ndi pwepwete kuchitekete teketeke nje
patenthe pelete tiime mphepete tiyale jekete zitenje
hook
(saxess)
moyo w-nga
chilichonse ndinaika pa yesu
ndipo sindidanda
kulikonse ndimayenda nayenso (-2)
(mista gray)
ndikaf–ka andilimbitsa (yesu)
ndikadwala andichilitsa (yesu) (-4)
verse two (mista gray)
munaona a yesu amatekeseka? ayi
munaona a yesu amatekeseka? ayi
azibambo malikhwelu nthungululu azimayi
chala mmwamba tiloze most high
mighty saviour protector comforter king of judah counselor hero
kuphatikiza zabwino zonse za mdziko kuchoselapo yesu ansala ziro
uko uko uko uko odi
ndi mwini m’godi silver ndi gold ndi zake kodi
njara choonadi ndi moyo mau akutelodi
anauka kwa kufa apse ntima helodi
ndilibe pulobulemu
vuto siine musandichitepo bulemu
yesu alandile ulemu
wandichosa pa bench wandiika mu game
bridge (saxess)
anthu ena amandifunsa zambiri
ati how do i manage to win
ndimangoulula
hook
moyo w-nga
chilichonse ndinaika pa yesu
ndimangoulula
sindidanda kulikonse ndimayenda nayenso
ndikaf–ka andilimbitsa (yesu)
ndikadwala andichilitsa (yesu) (-4)
كلمات أغنية عشوائية
- god module - lucid (reaper mix) كلمات أغنية
- tropes - feast your eyes كلمات أغنية
- da real gimic - dirty money كلمات أغنية
- tv·2 - kalundborgbåden كلمات أغنية
- cascada - madness (cj stone radio edit) كلمات أغنية
- apologetix - school of ours كلمات أغنية
- sun dragon (1960s duo) - look at the sun كلمات أغنية
- ygxtus - wadadadeng! كلمات أغنية
- coach peake - had 2 get her كلمات أغنية
- pacmantv & rondomontana - the str8 drop كلمات أغنية