kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

mario bro's (mw) - cup كلمات الأغنية

Loading...

[verse 1: crispy malawi]
runner dancehall zau masicka
mpasha kupanga kufaka pansika
unamva za bar yo pita m_th_lika
ndikomwe ndili pano man kutalika
ndungo rapper man ndikulalika
ndilimwamba man mitambo ndabandika
ati “spe iwe uzikhalika, osamajama yanga disk yokalika”
ta winner ndife tipatse cup
mfana wovaya bwera ndupatse map
drip on drip ndipatse cup
fame ukasunge kwanu, ife tipatse guap

[refrain: crispy malawi]
tipatse cup, ndipatse cup
ndipatse cup
ta winner ndife, tipatse cup

[verse 2: ace dirty]
mkati kwambiri tatulukamo
bwanji umadana ndi chulungamo?
dollar ya cosoma kugulira sneaker
chi beat chokoma kuphulitsa speaker, mazenene
ma kicks ndi chidendene
izi ndizachilengedwe huh
nabadwa chonchi, game ndi yawo, chaku mangochi
ndamgwira thako wagwira ntochi
she gettin’ technical ngati ndi soche
rap ndatenga ndipatse trap
gist ili bho ndipatse sharp
ma screenshot ayi ndipatse snap
mfana wothamanga ndipatse lap
[refrain: crispy malawi]
tipatse cup, ndipatse cup
ndipatse cup
ta winner ndife, tipatse cup

[verse 3: de zenzo]
a nusaince to the game, like serpant is p_rn[?]
f_ck your opinion, this is rap’s very own
dolo wako ndimupanga chandamale
while i’m smokin’ ndine dube, she f_ckin’ bob marley

[verse 4: krazie g]
effortless, leveless
the devil next city is heat that we droppin'[?]
don’t second guess i like pasta, nde eko verse
this tha vatican pope
ndipatse cup, the drip got it twisted
ndimpatse tap
ukandiyesa nde undipatse sup
kukonda mpasha koma simpatsa gap

[outro: krazie g ]
haa! ndipatse cup

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...