malumbo kondowe - ofunika ku worker كلمات الأغنية
verse 1
ndikaona komwe ndachokera
zomwe amkanena masten zija ndizomveka
mwana w_nga moyo siophweka
kuti ulimbe pa town zimafuna ku worker
osagona, k_menya tima hustle kuwonesetsa kuti chilichonse chikutheka
osaiwala mulungu patsogolo
tsiku ndi tsiku 2 dzina lake kulikweza
yeah! you really have to strive hard
if you really wanna make it this far
don’t rely too much on people
otherwise you will get yourself stressed out
limbikila school mwana w_nga
tizibwana moyo mu tachepetsa
ndimafuna mzaone utapanga gala
kenako ukuyendela ka sienta
chorus
ofunika ku worker
ngini singathеke utangokhala pansi neba
ghetto yuthi don’t strеss yeah
ingolimbikila one day zizatheka ah ah
ofunika ku worker
if you really wanna make the paper
(if you really wanna get the paper)
ghetto yuthi don’t stress yeah
ingolimbikila one day zizatheka
verse 2
there’s no shortcut to success
mwana w_nga ukufunika ku worker basi
sizofuna mpaka kukhetsa mwazi eti
ndicholinga choti uzaiphule fast
nah! making money is a process
pena umapeza nthawi zina ayi
osamapangaso za corruption
akazak_manga bail yako adzapereke ndani?
yeah! ndikamakamba zo worker eti
sitikutathauzatu ku vepi kokha
huh! you can be doing ka business
make sure it’s clean
osati ya illegal one
now
let’s get into the scriptures
timve amati chani zokhuza ku worker eti
genesis 3 verse yake ya 19
go and read it mukamva kuti ikuti chani
كلمات أغنية عشوائية
- ted nugent - hot or cold كلمات الأغنية
- heaven grey - the way back is gone كلمات الأغنية
- andrew garcia - dumb كلمات الأغنية
- firstborn - vajra eyes كلمات الأغنية
- tiamat - thunder & lightning كلمات الأغنية
- arsonists get all the girls - gooseknuckle كلمات الأغنية
- nana mouskouri - barbara furtuna كلمات الأغنية
- kanye west - knock knock (remix) كلمات الأغنية
- sublime cadaveric decomposition - controlling the rules of unequal trade كلمات الأغنية
- bruce dickinson - the ballad of mutt كلمات الأغنية