kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lawi - my child كلمات الأغنية

Loading...

[verse 1]
i am abused in many ways
and i have learned to live with the pain
everyday is a rainy day
is it because i’m a girl?
is it because i’m a girl?
musandichite nkhaza poti ndine mtsikana
somebody please help me
to break away from the hurting
i have known pain and fear
is it because i’m a girl?
is it because i’m a girl?

[chorus]
nthandizeni msanga poti moyo ukulemera ine mwana wamkazi (ndalira)
nthandizeni msanga ndimafuna nditaphunzira ndidziyimile ndekha (somebody please)
nthandizeni msanga poti moyo ukulemera ine mwana wamkazi (ndalira)
nthandizeni msanga ndimafuna nditaphunzira ndidzigulire ___
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
[verse 2]
musandichitе nkhaza poti ndine mtsikana
musandichite nkhaza poti ndine mtsikana
i’m a woman, queen of thе warm heart
intelligent, wise and beautiful
never underestimate the potential in me
i’m a believer in the power of dreams
and i won’t stop at nothing
let me be the woman i wanna be
is anybody out there?

[chorus]
nthandizeni msanga poti moyo ukulemera ine mwana wamkazi (ndalira)
nthandizeni msanga ndimafuna nditaphunzira ndidziyimile ndekha (somebody please)
nthandizeni msanga poti moyo ukulemera ine mwana wamkazi (ndalira)
nthandizeni msanga ndimafuna nditaphuzira ndidzigulire ___
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu
ufulu

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...