
lawi - mtengo lyrics
[verse 1]
kodi mwanayu akula bwanji opanda kholo?
nanga mwanayu aphuzira bwanji opanda mphuzitsi?
mapeto ache, oh, tamuluza yeah
mapeto ache, oh, tamuluza yeah
kodi mwanayu akula bwanji opanda kholo?
nanga mwanayu aphuzira bwanji opanda mphuzitsi?
mapeto ache, oh, tamuluza yeah
mapeto ache, oh, tamuluza yeah
[pre_chorus]
mukadzawuwonayi mtengo wadulidwa mizu, yeah
umawuma yeah, umawuma, mawuma yeah
mukadzawuwona mtengo wayoyola masamba yeah
ukuwuma yeah, ukuwuma, ukuwuma yeah
poti mtengo ukayoyola masamba yeah
ukayoyola masamba, yeah
umawuma, umawuma
[chorus]
mtengo ungakule bwanji opanda mizu?
nanga ungapume bwanji opanda masamba, yeah?
udzawuma yeah, udzawuma
udzawuma yeah, udzawuma
mtengo ungakule bwanji opanda mizu?
nanga ungapume bwanji opanda masamba, yeah?
udzawuma yeah, udzawuma
udzawuma yeah, udzawuma
[verse 2]
monga momwe mtengo usowa masamba, yeah
ndimomwe masamba asowera mtengo
tsamba likagwa mtengo uchita manyazi
zikhalira kudalirana mama, yеah
mtengo udalira nthaka, yeah
ndipo munthakamo mukhalemo madzi
imva mwanawе nzeru zozama, yeah
zipezeka mu mtengo wakachere
[pre_chorus]
mukadzawuwonayi mtengo wadulidwa mizu, yeah
umawuma yeah, umawuma, mawuma yeah
mukadzawuwona mtengo wayoyola masamba yeah
ukuwuma yeah, ukuwuma, ukuwuma yeah
poti mtengo ukayoyola masamba yeah
ukayoyola masamba, yeah
umawuma, umawuma
[chorus]
mtengo ungakule bwanji opanda mizu?
nanga ungapume bwanji opanda masamba, yeah?
udzawuma yeah, udzawuma
udzawuma yeah, udzawuma
mtengo ungakule bwanji opanda mizu?
nanga ungapume bwanji opanda masamba, yeah?
udzawuma yeah, udzawuma
udzawuma yeah, udzawuma
Random Lyrics
- ricky reyna - sigo bateando (prod. by hozay & maxx gallo) lyrics
- ginan atsy - nighttime lyrics
- young flex feat. maxis - keine zeit lyrics
- synnxr - run away lyrics
- ufell - caperusita lyrics
- alex rose - cuarentena* lyrics
- weezy (beats pharma music) - y'a pas de gala lyrics
- jc seals iii - she said yes lyrics
- $hirak & bokoesam - nuh like dat lyrics
- whiterosemoxie - mio lyrics