kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lawi - galimoto كلمات الأغنية

Loading...

[chorus]
galimoto, galimoto (ndidziti nkati break khwe miseche nayo balala)
galimoto, galimoto (mundigulire ine galimoto)

[verse 1]
ndimayenda wapasi ine eh_eh
minga zimandibaya ine eh_eh
anthu akandiona ine eh_eh
amayamba kuseka ine eh_eh

[refrain]
kodi dona yambwana iyo (siyo)
kubayika ndi minga iyo (siyo)
ngati makobidi kulibe kwawoko (siyo)
ndalema ndi chitonzo mundigulire, oh

[chorus]
galimoto, galimoto (ndidziti nkati break khwe miseche nayo balala)
galimoto, galimoto (mundigulire ine galimoto)
galimoto, galimoto (ndidziti nkati break khwe miseche nayo balala)
galimoto, galimoto (mundigulire ine galimoto)

[verse 2]
poti bambo ndinu namalamba mimbayi ndi umboni
m’mudzima nkhani akamakamba siyose ili miseche
muli ndi galimoto mumakwera mukafuna
nane ndi galimoto ndingathetse zolankhula
[refrain]
kodi dona yambwana iyo (siyo)
kubayika ndi minga iyo (siyo)
ngati makobidi kulibe kwawoko (siyo)
ndalema ndi chitonzo mundigulire, oh

[bridge]
sho sho, pee_pee
fumbi kuti lakata
sho sho, ka_kata boom, kata_kata bumba
vrrm, vrrm, pha
vrrm, vrrm_vrrm, pha

[refrain]
kodi dona yambwana iyo (siyo)
kubayika ndi minga iyo (siyo)
ngati makobidi kulibe kwawoko (siyo)
ndalema ndi chitonzo mundigulire, oh

[chorus]
(sho sho, pee_pee, sho)
galimoto, galimoto (ndidziti nkati break khwe miseche nayo balala)
galimoto, galimoto (mundigulire ine galimoto)
galimoto, galimoto (ndidziti nkati break khwe miseche nayo balala)
galimoto, galimoto (mundigulire ine galimoto)

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...