kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lawi - chifundo nane كلمات الأغنية

Loading...

[intro]
ayy
chifundo nane
chifundo nane
oh, chifundo nane
chifundo nane
chifundo nane
chifundo nane
mtima w_nga don’t you worry
everything is gonna be alright

[chorus]
ambuye ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
mtima w_nga sudera nkhawa
chif_kwa ali ndi chifundo nanee
ine mtima w_nga sudera nkhawa (oh no)
chif_kwa ali ndi chifundo nane

[verse 1]
machimo anga ndi ambirimbiri osawerengeka ndipo
mutazindikira zamumtima mw_nga mukhoza k_mandisala
m_th_ kufuna kundimangilira ndikundiponya mu m’ndende
ndizokoma kundiweruza, nzovuta kundimvetsetsa
ndiye amene anandipanga amandidziwa
zinsinsi zangazi pamaso pake ndizosabisika
koma ngakhale ndimachimwa iye andikondabe
amatsegura manja ake ndi kundik_mbatira
[chorus]
oh, ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nanе
mtima w_nga sudera nkhawa
chif_kwa ali ndi chifundo nanee
ine mtima w_nga sudera nkhawa (oh no)
chif_kwa ali ndi chifundo nanе (oh, yeah)

[verse 2]
ayi_yayi_yayi
ayi, ndachoka kutali, moyo w_nga ndi umboni
wandimenyera nkhondo, ndangokhala chete
pomwe adani anga andik_mbira mitsinje
wandimangira mlatho, ndayenda powuma
wandifewetsera zolimba zanga

[chorus]
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ine mtima w_nga (sudera nkhawa chif_kwa ali ndi chifundo nane)
ine mtima w_nga (sudera nkhawa
chif_kwa ali ndi chifundo nane)

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...