
langwan piksy - wako wako كلمات أغنية
verse 1
uthenga wa masankha kwa namazanje
panopa tiri official si za masanje
lero sitisamala za wansanje
tivine ingoma
mkhetekete ndi manganje
chorus
tinafunitsitsa banja t-tamanga
koma tinadziwa kufika si ku thamanga
ona lero ndine wako wako
ndine wako wako
ona lero ndine wako wako
ndine wako wako
verse 2
ulendo wathu tangoyamba komano tikafika
kaya mitunda tikwera ndi 0p t-tsika
tilowa pena mmatope pena tiponda minga
koma chimodzi ndikhulupira yehova ndi linga
tiyenda mu dzuwa
mvula
limodzi tikula
uk-mva?
namazanje
chorus
tinafunitsitsa banja t-tamanga
koma tinadziwa kufika si ku thamanga
ona lero ndine wako wako
ndine wako wako
ona lero ndine wako wako
ndine wako wako
verse 3
poti ndasankha iweyo kuti ndikupatse w-nga mtima
poti ndasankha iweyo kaya mokhwepa ndi mothina
honey ndasankha iweyo kaya kuwala kaya mdima
ine ndasankha iweyo kuti tikhale mpaka muyaya
ndasankha iwe
poti ndasankha iwe
poti ndasankha iweyo honey
ndasankha iweyo namazanje
chorus
tinafunitsitsa banja t-tamanga
koma tinadziwa kufika si ku thamanga
ona lero ndine wako wako
ndine wako wako
ona lero ndine wako wako
ndine wako wako
كلمات أغنية عشوائية
- harle - karma 1116 كلمات أغنية
- south strip - plenty كلمات أغنية
- çağrı sinci - lobotomi (groovypedia live) كلمات أغنية
- abby holliday - ohio laundry room كلمات أغنية
- bib sama. - bleed كلمات أغنية
- jc hipster - nightmares freestyle كلمات أغنية
- muslim (eg) - mabhtmesh | مابهتمش كلمات أغنية
- tery - не можу так (i can't do that) كلمات أغنية
- sinister s - amenaza nacional كلمات أغنية
- elunqu - опиаты (opiates) كلمات أغنية