langwan piksy - mphongo كلمات الأغنية
chorus
kufeela ngati mphongo (mphongo – mphongo)
nthaka ya chinyontho (mphongo – mphongo)
chikondi ngati k-ma loto (mphongo – mphongo)
kufeela ngati mfumu (mphongo – mphongo)
kutentha ndiri juuu (mphongo – mphongo)
verse one
mkazi w-nga ndi professional
chikondi chake chiri sensational
chikondi cha natural ma rehearsal no
easy….musazitenge personal
lol
chikondi chake ndikuopa chindinenepetsa poti chachuluka starch
kukhala naye sizitheka kungomuyang’ana i’m tempted to touch
ndimadziwa amandikonda asananene akachita kuyankhula nde nanji
chikondi chake ndi more..yes i’m feeling all good
chorus
kufeela ngati mphongo (mphongo – mphongo)
nthaka ya chinyontho (mphongo – mphongo)
chikondi ngati k-ma loto (mphongo – mphongo)
kufeela ngati mfumu (mphongo – mphongo)
kutentha ndiri juuu (mphongo – mphongo)
verse two
mkazi w-nga ali ndi vision
chikondi chake cho no season
amandikonda opanda reason
kusokoneza please no
ndimadziwa kusankha iye kuti akhale wa pa mtima sinnalakwitse yi
zikanakhala zimatheka bwenzi ndikukhala naye like everyday
okambawo amadziwa tilipobe no matter what they gonna say
we standing tall, lovings all the way
chorus
kufeela ngati mphongo (mphongo – mphongo)
nthaka ya chinyontho (mphongo – mphongo)
chikondi ngati k-ma loto (mphongo – mphongo)
kufeela ngati mfumu (mphongo – mphongo)
kutentha ndiri juuu (mphongo – mphongo)
verse three
(dan lu)
babe mvera ndiwe number one
pagulu la nzako umadya one
ndik-mva sugar
ndik-mva raga
it’s all good
(piksy – rap)
ndine mphongo yowilira
musatsutse ndi mmene ndiku feelira
ondifuna akuyenera kupilira
ndikufewa mafana mwandilira
vomerezani..mfana i’m rocking
jus lay back man lemme do the talking
yeah, ndik-mva kukoma
chofewa chimphongo chodziwika ndi boma
chorus
kufeela ngati mphongo (mphongo – mphongo)
nthaka ya chinyontho (mphongo – mphongo)
chikondi ngati k-ma loto (mphongo – mphongo)
kufeela ngati mfumu (mphongo – mphongo)
kutentha ndiri juuu (mphongo – mphongo)
كلمات أغنية عشوائية
- fc five - easy sentiments كلمات الأغنية
- firevision - look right through me كلمات الأغنية
- jesters funeral - private demon كلمات الأغنية
- serge lama - dis pedro كلمات الأغنية
- elvis presley - suppose كلمات الأغنية
- frank sinatra - as you desire me كلمات الأغنية
- gathering - black light district كلمات الأغنية
- elton john - a dream come true كلمات الأغنية
- gene watson - ain't no fun to be alone in san antone كلمات الأغنية
- finger eleven - dropping كلمات الأغنية