kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

langwan piksy - everyday كلمات الأغنية

Loading...

ati ndiri mchikondi… well… that’s obvious
sikuti ndazelezeka… chikondi basi
awesome palibe kutinamizayi
made in heaven palibe kukakamiza ayi
i look at you and i sekelera
you complete me kupanda iweyo i pelewera
ukakhalapo no chovuta
wandithesera kufuntha
ukathyali wonse wafufuta
listen
zikundivuta kubisa
zikundivuta kubisa-la
oh no
i wanna tell
i wanna sing
i want the whole world to see
and know
w-nga ndiwe coz i’m so sure
moyo uchuluka ma ups and downs
but i promise i’ll always be around
chiri chonse is gonna be okay
sinduchoka honey i’m staying

chorus
ndikungogwabe mchikondi nawe
everyday
ndikungogwabe mchikondi nawe
everyday

pakusankha iwe p-n-libe mistake
zokonda zanga umachita respect
tiye
ndigwire
khalidwe lako undigaire
unamva za mbirimbiri still u trust me
ndimasakabe pano ndakhala pansi
you my best friend
nd bwenzi
i thank god for you sugar you amazing!
this feeling ndiri nayo njachilendo
mwina nyengo
poti ambiri akutero
linali pempho
kuti ndidzapange settle
with an angel
now i know god is able

moyo uchuluka ma ups and downs
but i promise i’ll always be around
chiri chonse is gonna be okay
sinduchoka honey i’m staying

chorus
ndikungogwabe mchikondi nawe
everyday
ndikungogwabe mchikondi nawe
everyday

cholinga changa tidzafike banja
tsono dekha usakaike nzanga

nkhawa zako udzinena
ndipo tidzipemphera
sionse akondwera
tiri muchikondi honey

you so natural. . full of action
ndimadziwa umandikonda nkayang’ana mmaso
when you smile b-ssop
i just wanna kiss yah
kukhala nawe moyo w-nga wonse ndifunitsa

moyo uchuluka ma ups and downs
but i promise i’ll always be around
chiri chonse is gonna be okay
honey im staying

chorus
ndikungogwabe mchikondi nawe
everyday
ndikungogwabe mchikondi nawe
everyday

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...