kwemogoon - bestie wa tay grin كلمات الأغنية
[intro]
(i_i_it’s t h u g records)
[chorus]
tay grin aise nde ndi bestie
amabwera kwathu daily chama three
m’mangolubwalubwa simudziwa gist
mfumu ya zinyawu ndi bestie
ukawona missed call amakhala ndi dirty
major one yake ija, afuna anditenge
best friend wa tay grin
best friend
best friend wa tay grin
best friend
[verse 1]
bestie aise
siticheza mosiyana
bestie aise
timavaya kwa tiana
kuvaya pa benz ina tiye pa beemer, yah
amandiuza zizayenda tsiku lina
kaya muzidisa, koma ifeyo timamvana
mix tangofika nde ma guy amatisata
timavaya jones ndeno bas kukango trapper
osadabwa ukandiwona ineyo ndikunjanja
ndungosaka cash
ku baller ndima friends
kuvayano pa spot kukangotsila ndima babes
sitivaya geli, dollar sitidyera break
patokhaso ndife zima blesser
[chorus]
tay grin aise nde ndi bestie
amabwera kwathu daily chama three
m’mangolubwalubwa simudziwa gist
mfumu ya zinyawu ndi bestie
ukawona missed call amakhala ndi dirty
major one yake ija, afuna anditenge
best friend wa tay grin
best friend
best friend wa tay grin
best friend
[verse 2]
bestie wa tay grin nde ineyo, yah
tungosegula ka label nde ifeyo
kugawano zi gin
amabweretsa zi lin
timbizi tanu kwa ifeyo timabwera
sitigwera
koma aise tili lit
takugwetsa m’bar imozi tawona suli fit
kufilisa guys ife nde ndi gist
sunganyoze ifeyo pali gulu
bro dat nde ndi risk
kugwetsa hit ndi my bestie
kuyika fit ndi tay grin
kugwetsa hit ndi my bestie
kuyika fit ndi tay grin
[chorus]
tay grin aise nde ndi bestie
amabwera kwathu daily chama three
m’mangolubwalubwa simudziwa gist
mfumu ya zinyawu ndi bestie
ukawona missed call amakhala ndi dirty
major one yake ija, afuna anditenge
best friend wa tay grin
best friend
best friend wa tay grin
best friend
كلمات أغنية عشوائية
- sneaker pimps - roll on (line of flight mix) كلمات الأغنية
- 4n way & fendiglock - oxywatch كلمات الأغنية
- cartier'god - stars كلمات الأغنية
- erna džeba - cunami كلمات الأغنية
- o pombo - sem você كلمات الأغنية
- deathbyromy - even if it bleeds كلمات الأغنية
- garolou - la vendée كلمات الأغنية
- esham - circle of sloth كلمات الأغنية
- keane - bedshaped (demo) [fierce panda single 2] كلمات الأغنية
- жулик (swindler) - мантры (mantras) كلمات الأغنية