king tuzi & crispy malawi - tuno كلمات الأغنية
[intro: king tuzi]
“amwene”
“amwene ineyo ndikangomulingalira tuno amwene”
“ehe ukamulingalira tuno chimachitika ndi chani
abdul with the sauce
“ndikangoti ndimuganizire tuno amwene”
“ukangoti umuganizire tuno chimachitika chani?”
“iwe tayankha eh”
“tasiya kubanda tayankha”
“amwene golide amwene golide eh tuno amwene”
“golide wotani?”
“ndikangoti ndimuganizire tuno amwene” (ayy)
“ndikati golide yokhayo” (ayy)
(ayy)
[chorus :king tuzi]
ndapota ka spliff kukayatsa (eish)
kundilowa mphuno (utsi) (amwene)
ndaona chimkazi (mmh hm) ali welo (mmh hm)
ndikufunika chi cross ngati bruno (ndipatsile chi cross) (ayy ay)
ndilipa magobo daily
osamabwelela mbuyo (osamabwelela mbuyo)
they were sleeping on me now amwayi adzuka
koma ena akadali mtulo
i got a confession i’m crushing on tuno (eish) (eh) (eh) tuno!(eh)
tuno! (koma tuno ase) (amwene)(mmh)
tuno!
(koma tuno ase) ndati ndaona chi mkazi ali welo
kufunika chi cross ngati bruno (eh amwene)
chi chick cha bho ngati afuna banja (eish) (eish)
muwuze andipeze kuno (tiye nazo)
(ayy)
(ayy)
[verse 1 : king tuzi]
tuno
amwene (amwene) ntagwira uyuyu ndingapenge (ndingapenge) (eish)
ma member ati ndumayabwa
akangomva da king ngati aponda chitedze (ngati ndaponda chi cha?)
tuzi ku flopper man sizingatheke
ndayenda ndi ganja ndukakwera ndege
zosatheka
ndimapusha zitheke
she[?] didn’t want to feature these rappers keep begging (let’s go)
ndine mfana wofewa (ofewa) nsima ndimamwera fanta (fanta)
koma sumandisala spaghetti (sumandisala)
ndine mfana wozungiza bongo rasta
sindiwopa kuvaya ku ndende (sindiwopa kuvaya)
koma ndendende
sak_mvetsetsa i’m stoned
ati ah ukufuna umgende? (ah)
zandi wenger ngati coach wa _rs_nal
muyimbire spe afika anditenge (muyimbire spe)
ndati tuno alikuti? (alikuti)
in the trap see the way i be rapping
they say i’m the goat ati tuzi ndi mbuzi (sikunyoza ayi)
lil shorty bad and she boujee
let her meet the fam
kudzamutenga k_mudzi
and i just hit another but no dey ain’t no strings attached
palibepo ulusi (palibepo ka cha?)
ndili pa tv pa news (uti bwa?)
i’m the goat when it comes to the music
[chorus : king tuzi]
ndapota ka spliff kukayatsa (eish)
kundilowa mphuno (utsi) (amwene)
ndaona chimkazi (mmh hm) ali welo (mmh hm)
ndikufunika chi cross ngati bruno (ndipatsile chi cross) (ayy ay)
ndilipa magobo daily
osamabwelela mbuyo (osamabwelela mbuyo)
they were sleeping on me now amwayi adzuka
koma ena akadali mtulo
i got a confession i’m crushing on tuno (eish) (eh) (eh) tuno!(eh)
tuno! (koma tuno ase) (amwene)(mmh)
tuno!
(koma tuno ase) ndati ndaona chi mkazi ali welo
kufunika chi cross ngati bruno (eh amwene)
chi chick cha bho ngati afuna banja (eish)
muwuze andipeze kuno (eish)
(ayy)
(ayy)
[verse 2 : crispy malawi]
(malawian)
uli ndi thako kapena umangotha kugwedeza chiuno(hmm?)
kuyika dollar pa table kuti ndikutengere ku bedi ngati tulo
koma sindikuthoka iweyo tuno
ndikufuna nzako wachi mbuyo (wachi mbuyo)
ati spe ma babe umangosintha ngati kicks
kodi umamenya judo?
hmm
keep it going keep it moving (vroom vroom)
ngati sizikuyenda yatsa ma hazard
zathu zikuyenda tika dropper anthu amangoti ah za hard (waona)
zili fly ngati nthakati[?]
ku north,k_mwera ndi pakati (yeah)
been a player kwa zaka zaka
pano level yang_yi ndi ya lampard
ma drinks titha ku shoppa
ma mogo amandipweteka mphuno (mmh) (tuno)
utha kushala panja
ukapota spliff ndi kuzayatsila muno (tuno)
koma na lero olo nepman sanakambaso za dzulo?(no way)
ife nde tili mkati
uli panja udya bench ngati ukunyamula zitsulo
(yeah)
[chorus :king tuzi]
ndapota ka spliff kukayatsa (eish)
kundilowa mphuno (utsi) (amwene)
ndaona chimkazi (mmh hm) ali welo (mmh hm)
ndikufunika chi cross ngati bruno (ndipatsile chi cross) (ayy ay)
ndilipa magobo daily
osamabwelela mbuyo (osamabwelela mbuyo)
they were sleeping on me now amwayi adzuka
koma ena akadali mtulo
i got a confession i’m crushing on tuno (eish) (eh) (eh) tuno!(eh)
tuno! (koma tuno ase) (amwene)(mmh)
tuno!
(koma tuno ase) ndati ndaona chi mkazi ali welo
kufunika chi cross ngati bruno (eh amwene)
chi chick cha bho ngati afuna banja (eish)
muwuze andipeze kuno (eish)
(ayy)
(ayy)
كلمات أغنية عشوائية
- hideandseekzoo - 7 كلمات الأغنية
- רביד פלוטניק - yamim yagidu - ימים יגידו - ravid plotnik كلمات الأغنية
- claver gold - l'orbita كلمات الأغنية
- yung spitta - intro كلمات الأغنية
- prophloc - rdsz(prawdziwe wersy) كلمات الأغنية
- massa moon - muse كلمات الأغنية
- make dollars not sense (mdns) - money on my mind كلمات الأغنية
- lildanny - не такой как ты / lgыn diss كلمات الأغنية
- yüth forever - bitterromantic, pt. 3 كلمات الأغنية
- westside gunn & conway - rahbannga كلمات الأغنية