kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

kineo madness, aidfest madness & zeze kingston - anzanu كلمات الأغنية

Loading...

[intro:kineo & zeze kingston ]
ayo! billy
hmhihihi serato
aye
aye
aye
aye
(ayo tiyeni!) aye ay
ayy ay (tiyeni! tiyeni! tiyeni!) ay ay (eish!)

[verse 1: kineo]
koma awa kulongolola
koma awa kulongolola
matukutuku adzawapweteka (pweteka)
matukutuku adzawapweteka (mmh)
koma awa kulongolola
koma awa kulongolola (iyee iye)
matukutuku adzawapweteka (ayiyaya ya)
matukutuku adzawapweteka (ayiyaya ya)
umangolonjeza
koma kanthu suchita
koma inu kunamiza
kutipusitsa
umangolonjeza,koma kanthu suchita (iyee iye)
iwe koma kunamiza
k_mangotipusitsa
[pre_chorus: aidfest]
umangotilonjeza (iyee), umangotipusitsa (iyee)
umangotinamiza (iyee), umangotinamiza (iyee)
umangotilonjeza (iyee), umangotipusitsa (iyee)
umangotinamiza (iyee), umangotinamiza (iyee)
washii!

[chorus : aidfest]
anzanu anzanu amangochita anzanu
salubwalubwa anzanu, amangochita anzanu
anzanu anzanu amangochita anzanu
salubwalubwa anzanu, amangochita anzanu
anzanu anzanu amangochita anzanu
salubwalubwa anzanu, amangochita anzanu
anzanu anzanu (ay!) amangochita anzanu (ay!)
salubwalubwa anzanu (ay!),amangochita anzanu. (ay!)

[post_chorus :kineo]
iyee
iye iyee
iyee
iye iyee
iyee (ayo tiyeni!)
iye iyee
iyee (tiyeni! tiyeni! tiyeni! eish!)
iye iyee
[verse 2: zeze kingston]
mwanena ichi, mwanena ichi
ife timangongo k_mverani
koma mumangolubwa sumumachita
mwati mukupusitsa ndani?
mwanena ichi, mwanena ichi
ifе timangongo k_mverani
koma mumangolubwa sumumachita
mwati mukupusitsa ndani?
koma mumati abwanawo kuno ndi azoba iwo
khalidwe lawo ndilopusa iwo
abwanawo kuno ndi azoba iwo
khalidwe lawo ndilopusa iwo

[pre_chorus: aidfest]
amangotilonjеza, amangotipusitsa
amangotinamiza,amangotinamiza
umangotilonjeza,umangotipusitsa
umangotinamiza, umangotinamiza
washii!

[chorus : aidfest]
anzanu anzanu amangochita anzanu
salubwalubwa anzanu, amangochita anzanu
anzanu anzanu amangochita anzanu
salubwalubwa anzanu
amangochita anzanu
anzanu anzanu amangochita anzanu
salubwalubwa anzanu, amangochita anzanu
anzanu anzanu (ay!) amangochita anzanu (ay!)
salubwalubwa anzanu (ay!), amangochita anzanu (ay!)
washiii
[post chorus: aidfest]
umangolonjeza
koma kanthu suchita
koma kanthu suchita
koma kanthu suchita
umangolonjeza
koma kanthu suchita
koma kanthu suchita
koma kanthu suchita
umangolonjeza
koma kanthu suchita
koma kanthu suchita
koma kanthu suchita
umangolonjeza
koma kanthu suchita
koma kanthu suchita
koma kanthu suchita
umangolonjeza
koma kanthu suchita,koma kanthu suchita,koma kanthu suchita
washiii!

[outro]
ish!, ish!, eh!
ish!, ish!
ih!,ih!,ih!, ih!
washiii!
washiii!

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...