kev'wayi - sitipita. كلمات الأغنية
intro (kev’wayi)
yeyo yoh kev you got it on point
yeyo, nthawi ilipo
verse
aseeh, sitipita
mpaka mpaka mawa, (yeyo yeyo)
aseeh, sitipita
tiku tikukhala, (nthawi ilipo)
aseeh, sitipita
mpaka mpaka mawa (yeyo)
aseeh, sitipita
tiku tikukhala (nthawi ilipo)
hook
sitipita (yeyo yeyo), sikunade (ayayah)
sitipita (okay okay), sikunade (yeyo yeyo)
sitipita (nthawi ilipo), sikunade (yosayamba)
sitipita (nthawi ilipo), sikunade (yeyo yeyo)
inu kwathuko, tatsanzika kuti tipita mawa (yeyo yeyo)

mmakwathumo, tatsanzika kuti tipita mawa (yeyo yeyo)

verse 1 (phill tee)
barman ndipatse folo
ndikufuna wa m’botolo
lero ndayaka lero ndablanda
ndikufunika dotolo
alasi avine, ma guys wa afile
paja ndine bayala
nkazi mmodzi ndipane
ngat ndine playala
sindikuchoka, sindikuf__ka
pano patelera
sindikudoja, sindikujoka
pano tichezera
pa stage ngati pakukwеla phill tee
pano sitichoka
ndawona nkazi osalala
koma ndi njoka ndeno ndati
hook (kev’wayi)
sitipita (yeyo yеyo), sikunade (ayayah)
sitipita (okay okay), sikunade (yeyo yeyo)
sitipita (nthawi ilipo), sikunade (yosayamba)
sitipita (nthawi ilipo), sikunade (yeyo yeyo)
inu kwathuko, tatsanzika kuti tipita mawa (yeyo yeyo)
inu kwathuko, tatsanzika kuti tipita mawa (yeyo yeyo)
mmakwathumo, tatsanzika kuti tipita mawa (yeyo yeyo)
mmakwathumo, tatsanzika kuti tipita mawa (yeyo yeyo)
verse 2 (kev’wayi)
yeyo yeyo
yeyo yeyo okay
from ten past to half past ma guy sitichoka (yeyo yeyo)
cha mma twenty to, cha mma quarter to, ma guy sitifoka (yeyo yeyo)
from half past to ten past ma guy sitichoka (yeyo yeyo)
cha mma twenty to, cha mma quarter to, ma guy sitifoka//
hook
sitipita (yeyo yeyo), sikunade (ayayah)
sitipita (okay okay), sikunade (yeyo yeyo)
sitipita (nthawi ilipo), sikunade (yosayamba)
sitipita (nthawi ilipo), sikunade (yeyo yeyo)
inu kwathuko, tatsanzika kuti tipita mawa (yeyo yeyo)
inu kwathuko, tatsanzika kuti tipita mawa (yeyo yeyo)
mmakwathumo, tatsanzika kuti tipita mawa (yeyo yeyo)
mmakwathumo, tatsanzika kuti tipita mawa (yeyo yeyo)
verse 3
yeyo yeyo
yeyo yeyo okay
from ten past to half past ma guy sitichoka (yeyo yeyo)
cha mma twenty to, cha mma quarter to, ma guy sitifoka (yeyo yeyo)
from half past to ten past ma guy sitichoka (yeyo yeyo)
cha mma twenty to, cha mma quarter to, ma guy sitifoka
aseeh, sitipita
mpaka mpaka mawa
aseeh, sitipita
tiku tikukhala
aseeh, sitipita
mpaka mpaka mawa
aseeh, sitipita
tiku tikukhala
aseeh, sitipita
mpaka mpaka mawa (yeyo yeyo)
aseeh, sitipita
tiku tikukhala (yeyo yeyo)
aseeh, sitipita
mpaka mpaka mawa (yeyo yeyo)
aseeh, sitipita
tiku tikukhala (yeyo yeyo)
hook
sitipita (yeyo yeyo), sikunade (ayayah)
sitipita (okay okay), sikunade (yeyo yeyo)
sitipita (nthawi ilipo), sikunade (yosayamba)
sitipita (nthawi ilipo), sikunade (yeyo yeyo)
inu kwathuko, tatsanzika kuti tipita mawa (yeyo yeyo)
inu kwathuko, tatsanzika kuti tipita mawa (yeyo yeyo)
mmakwathumo, tatsanzika kuti tipita mawa (yeyo yeyo)
mmakwathumo, tatsanzika kuti tipita mawa (yeyo yeyo)
eyo kings
كلمات أغنية عشوائية
- vilma alina - vainu كلمات الأغنية
- dudek p56 - to ludzie كلمات الأغنية
- jack cheshire - visitations كلمات الأغنية
- american ethos - marsyas versus apollo كلمات الأغنية
- sketching youth - let me go كلمات الأغنية
- blindagem - legião de anjos كلمات الأغنية
- sharkboy - on da edge كلمات الأغنية
- aiko el grupo - amigos para nunca (confía y te la lían) كلمات الأغنية
- outroeu - nós dois كلمات الأغنية
- bear kinggg - имею драг при себе (i have a drug with myself) كلمات الأغنية