kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

kelvin sings - rosalia's prayer كلمات أغنية

Loading...

[verse 1]
mwana uyo akuswereyo
ameneyo mumusunge bwino
lilime lake ndi lofewerako
ameneyo mumutenge bwino
akatopa ah (muloleni agone)
akathodwa ah (mpatseni madzi anga)
ndi mfumu mwana ameneyo (mufasa)
adzalamulira inu osamutola
mkati mwa iye muli nyimbo, podutsa pakati pa ziphinjo
mwanayo adzayimba eh, eh (adzayimba eh, eh)
inu ameneyo adzayimba, eh eh (adzayimba eh)
nyimbo za chimwemwe pa misozi yanu
zolimbitsa mitima yanu
phambe wampanga vessel, yonyamula uthenga wa bwino

[chorus]
musamulekelere mulereni, lereni (mu lеreni, lereni)
mulеreni, lereni (mu lereni, lereni)
mundilerere mwanayo poti akula nditatsetseleka
mu lereni, lereni

[verse 2]
osamuyang’anira pansi kamba ka kuchepa kwa phazi
he’s got big shoes to fill (big shoes to fill)
akalakwitsa mudzudzuleni mwa chikondi
akalapitsa osamumana chikoti
adziwe moyo ndi choncho, kuti nchito zibala zipatso
so he better work hard (work hard), keep his eyes on his record (record)
nothing will come easily, remind him to pray for his favour
don’t you look no further, ndinakukonda kale
usachite kupempha, anapeleka kale
bambo ako amulengalenga, wacholinga pokulenga
yemwe wakupanga vessel yonyamula uthenga wa bwino
[chorus]
musamulekelere mulereni, lereni (mu lereni, lereni)
mulereni, lereni (mu lereni, lereni)
mundilerere mwanayo, poti akula nditatsetseleka
mu lereni, lereni

[outro]
mundilerere mwanayo, adzatchuka nditayiwalidwa

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغنية الشائعة حالياً

Loading...