kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

kelvin sings - be praised كلمات أغنية

Loading...

[intro]
iwe, inva
iwe, inva
iwe, inva

[verse 1]
mumatenga zosweka, ndikuzikongoletsa
mwaitana osachera ndikuwalondera, yaweh
so let my everything follow yaweh

[pre_chorus]
ine sindingalore, kuti nsembe yanu ingopita pachabe
sindingalore, kuti nsembe yanuyo ingolowa m’madzi
nde ndi moyo w_ngawu, ndi luso langali
ndi zochepa zangazi, oh i give it to you, yaweh

[chorus]
be prasied (ndi moyo w_ngawu)
be praised (ndi zochepa zangazi) (oh)
inu mutamandike
mutamndike (oh)
be prasied (ndi moyo w_ngawu)
be praised (ndi zochepa zangazi) (oh)
inu mutamandike
mutamndike (oh)
[verse 2]
for everything you mean to mе, yeah
so lord you deservе all my prasies
you’ve been good to me, yeah
so lord i’ll exort you over all
misomali itatu ndikupulumutsa moyo w_ngawu
nde palibe chuma ndingapeleke kuposa moyo w_nga

[pre_chorus]
ine sindingalore, kuti nsembe yanuyo ingopita pachabe
sindingalore, kuti nsembe yanuyo ingolowa m’madzi

[chorus]
be prasied (ndi moyo w_ngawu)
be praised (ndi zochepa zangazi) (oh)
inu mutamandike
mutamndike (oh)
be prasied (ndi moyo w_ngawu)
be praised (ndi zochepa zangazi) (oh)
inu mutamandike
mutamndike (oh)

[outro]
mutamndike (oh)
tamandike (oh)
oh, oh yeah
mutamndike (oh)
tamwndike (oh)
(ndi moyo w_ngawu)
(ndi zochepa zangazi)

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغنية الشائعة حالياً

Loading...