
kelvin sings (mw) - manjenje كلمات أغنية
[intro]
mm, yeah, yah
[verse 1]
ukadzuka m’mamawa nkuyamika yehova (yehova, yah)
nk_mudalira kuti mavuto ako awasowa (awasova)
ebeneza, ndikutali wakuchotsa, yeah, yeah
pakamwa pako matamando osasosa, yah
[chorus]
amakuwopa awa, oh_no_no
amachita manjenje, oh_no_no, no_no, no_no
amakuwopa, awo, yeah, oh_no_no_no
amachita manje_, amanjenjemela nawe
[verse 2]
mavuto opanda kuwapempherera
ndyelekezi akawona zotelezi amasekelela, yeah
akondwera akawona kuti ku tchalitchi watenga tchuti, yeah
m’maganizo sungatsutsike m’mayesero akati alunjike
ukagwadwa ndikupemphera, k_midima k_matekeseka
ukamudziwa namalenga, ndizovuta kutekeseka
[pre_chorus]
poti nkhondo uk_menya pansipo anawina kale yawe
ukasiya kuyenda ndidziko nk_mayenda naye yawe
[chorus]
amakuwopa awa, no_no_no_no
amachita manjenje, oh_no_no_no_no
amakuwopa awo, oh_no, no_no, no_no
amachita manjenje, amanjenjemela nawe
[verse 2]
poti kupempheraku ndi nkhondo (rethe)
adani satopa kuzinga mikondo
pambuyo payesuyo londo
you already know zikavuta ndimagwada pama_
kuyitanila conqueror
nchipululu simokhala
palibe chomulaka
azaveka adani juzi mu october, yeah
you’re royalty, vala chisoti chako
the rest is vanity, iwe izi sizako
[pre_chorus]
poti nkhondo uk_menya pansipo anawina kale yawe
ukasiya kuyenda nk_mayenda naye yawe
[chorus]
amakuwopa awa,yah , no_no_no_no
amachita manjenje, oh_no_no, no_no
amakuwopa, awo, oh_no, no_no, no_no
amachita manjenje, amanjenjemela nawe
[bridge]
akazindikira what the almighty has inside of you
napepe, oyipayo amagwidwa manjenje
napepe, oyipayo amagwidwa manjenje
napepe, oyipayo amagwidwa manjenje
[chorus]
amakuwopa awa,yah , no_no_no_no
amachita manjenje, oh_no_no, no_no
amakuwopa, oh_no, no_no, no_no
amachita manjenje, amanjenjemela nawe
[outro]
amakuwopa, awo (woo)
amachita manjenje (yeah)
amakuwopa awo
amachita manjenje, manjenjemela
كلمات أغنية عشوائية
- bleauisnotcool - hunnit dolla bills كلمات أغنية
- supreme ag47 - ascension remix كلمات أغنية
- romantic punch - 화성에서 만나요 (life on) كلمات أغنية
- białas & lanek - noah كلمات أغنية
- the kite string tangle - mistakes to make كلمات أغنية
- broder john - snacket كلمات أغنية
- dehesa - contra suposto كلمات أغنية
- the searchers - popcorn double feature كلمات أغنية
- abis - la rue c'est brutale كلمات أغنية
- pejmaxx - j'bosse à mon compte كلمات أغنية